
Ulamuliro wa a Chakwera waonetsa chidwi chothana ndi katangale, atero a Chizuma
A Martha Chizuma omwe ndi mkulu wabungwe lothana ndi katangale la Anti-Corruption Bureau (ACB) ati utsogoleri wa a Lazarus Chakwera waonetsa chidwi chothana ndi katangale m'dziko la Malawi. Mkulu wabungweli amayankhula izi ku nkumano omwe… ...