
Amwalira nyumba itayaka moto
Mwana wa zaka ziwiri wamwalira m'boma la Mangochi atapsa modetsa nkhawa nyumba yomwe amakhala itayaka moto. Potsimikiza za ngoziyi, ofalitsa nkhani ku polisi ya Monkey-Bay, Alice Sichali, wati nyumbayi idayaka kamba ka mafuta a galimoto… ...