
Lulu ndi okula mtima – JB
Oyimba HipHop yemwe akukhala ku America, Jolly Bro, wati akuona kuti udani wakhoswe ndi mphaka omwe wayambika pakati pa iye ndi oyimba mzake Lulu siwutherapo ponena kuti Lulu ndiokura mtima, sakufuna kugonja. Jolly Bro yemwe… ...