
M’busa atsindika malemba molakwika pa mwana wa zaka 16
Apolisi kwa Mpingu m'boma la Lilongwe akusunga mchitolokosi mbusa wa mpingo wa Kadziyo Disciples, a Mccrystal Charlie a zaka 56, chifukwa chogonana ndi kuchimwitsa mtsikana wa zaka 16. Malingana ndi ofalitsa nkhani za apolisi ku… ...