Lamulo ligwire ntchito pa aliyense posatengera kuti ndi ndani – Chakwera
Mtsogoleri wa dziko lino Lazarus Chakwera wati aliyense amene akuchita zozunza anzake m’dziko muno lamulo ligwire ntchito pa iye. Chakwera wayankhula izi pa mwambo wokhazikitsanso kampeni yothana ndi matenda a Cholera komanso Covid-19 ndinso matenda… ...