Simulandira malipiro ngati simuyambaso ntchito – ogwira ntchito ku khothi auzidwa
Anthu ogwira ntchito ku mabwalo a milandu m’dziko muno ali pa chiopsezo chosalandira malipiro a mwezi uno ngati sabwelera ku ntchito msanga. Izi ndi malinga ndikalata yomwe boma latulutsa yomwe yasayinidwa ndi mlembi wamkulu wa… ...