![](https://malawi24.com/wp-content/uploads/2020/04/jAPPIE-235x176.jpg)
Chiwelengero cha opezeka ndi Corona chafika pa 101
Ku Malawi, chiwelengero cha anthu omwe apezeka ndi kachilombo ka Corona komwe kakumayambitsa matenda a Covid-19 chafika pa anthu 101 tsopano. Watsimikiza za nkhaniyi ndi nduna ya zaumoyo m'dziko muno a Jappie Mhango omwe amayankhula… ...