Samalani chakudya, kuli njala- Joyce Banda
Mtsogoleri wakale wa dziko lino, Joyce Banda, walangiza mzika za dziko lino kusamala chimanga kamba ka njala yoopsa yomwe iyale mphasa chaka chino chifukwa cha kusintha kwa nyengo. A Banda ayankhula izi Lachitatu ku Domasi… ...