Kuno mathanyula ayi, zatelo nzika zokhudzidwa
Gulu la anthu ena omwe akuzitchula kuti nzika zokhudzidwa, zati sizoyenera kuti dziko lino liziloleza maukwati amuna kapena akazi okhaokha. Poyankhula ndi tsamba lino, mmodzi mwa mzika zokhudzidwazi a Edward Kambanje omwe ndi wa chiwiri… ...