Abambo ambiri sanayezetse magazi, atsikana achichepere akutenga HIV kwambiri – yatelo NAC
Bungwe lotsogolera ntchito yolimbana ndi matenda a Edzi la National Aids Commission (NAC), lati kafukufuku akuonetsa kuti a bambo ambiri akumangodziyendera osayezetsa magazi pomwe akuti atsikana a chichepere makamaka m'sukulu zaukachenjede ndi omwe akutenga kwambiri… ...