CAMA yaikira kumbuyo ganizo lokweza mitengo ya mafuta
Bungwe loyang'anira ufulu wa anthu ogula m'dziko muno la Consumers Association of Malawi, (CAMA) laikira kumbuyo ganizo laboma lofuna kukweza mitengo ya mafuta a galimoto. Izi zikutsatira mphekesera yomwe yakhala ikuveka posachedwa yoti boma litha… ...