Marinica wati sakutula pansi udindo
Anthu omwe amayembekeza kuti awona m'phunzitsi watimu ya dziko lino Mario Marinica akutula pansi udindo kaamba kakusachita bwino kwa timuyi alemba m'madzi ndipo achule awerenga kaamba koti m'phunzitsiyu wati sangapange chibwana chamchombo lende ngati chimenecho.… ...