
2025 NBS Bank Charity Shield yaphula K66.8 million
Nkhondo ya masewelo a mpira wa miyendo yomwe inalipo Loweluka lathali pakati pa Silver Strikers ndi Mighty Wanderers mu mpikisano wa 2025 NBS Bank Charity Shield yakwanitsa kupanga ndalama zokwana 66.8 million Kwacha, masewelo omwe… ...