![Edgar Lungu](https://malawi24.com/wp-content/uploads/2016/05/Edgar-Lungu-235x176.jpg)
Zitengera a Malawi kukavotera mtsogoleri wanzeru – Watero Lungu
M'tsogoleri wakale wa dziko la Zambia, a Edgar Chagwa Lungu, wati zitengera a Malawi kukavotera m'tsogoleri amene ndi wongoyeselera zinthu kapena wodziwa zinthu, maka pachisankho chomwe chichitike chaka chamawa m'dziko muno. A Lungu ayankhula izi… ...