UDF ndi UTM zati MCP yapereka ndalama ndi ufa kwa anthu odzaponya voti
Zipani za United Democratic Front (UDF) ndi UTM zadandaula kuti chipani cha Malawi Congress Party (MCP) chimapereka thumba la ufa lolemera 25 kilogalamu komanso ndalama kwa anthu omwe aponye voti pachisankho chachibwereza pa 26 September… ...