Chiyembekezo cha a Malawi chikhale mwa a Chilima – atero a Kaliati
Patricia Kaliati yemwe ndi mlembi wamkulu wa chipani cha UTM wauza a Malawi kuti akuyenera kuyika maso komanso chiyembekezo pa a Saulos Chilima yemwe ndi mtsogoleri wachipanichi. A Kaliati amayankhula izi dzulo m'boma la Kasungu… ...