Makampani opanga mafuta ophikira atsitsa mitengo ya mafuta mwezi wamawa
Boma la Malawi kudzera ku unduna wa zamalonda lati makampani onse opanga komaso kugulitsa mafuta ophikira mdziko muno avomera kuti atsitsa mitengo kuyambira pa 1 mwezi wamawa. Izi zadziwika potsatira mkumano omwe boma linapangitsa sabata… ...