Misonkho ya a Malawi: Ma alawasi abowoka ku UNGA
Pomwe a Malawi ochuluka akudandaula za mavuto adzaoneni pankhani ya zachuma, anthu omwe aperekeza mtsogoleri wa dziko lino a Lazarus Chakwera ku nsonkhano wamayiko (UNGA), akhala akupuma moyo wina akabwera kumudzi kuno, pomwe malipoti akusonyeza… ...