Duncan ndi mamuna wabwino – watelo Tamia Ja
…wati osamayankhulitsa chibwezi chikatha Akayanjana: patangodutsa sabata zochepa ochita zisudzo Tamia Ja atasambwadza bwenzi lake Duncan Nyoni kuti ndi owumira, pano awiriwa abwelerana ndipo mkaziyu wayamikira kuti mamunayu ndi wabwino kwambiri. Kuyambira sabata yatha pakhala… ...