Longezani muzipita ku Ndata – Mia auza a DPP
Ati kwawo kwatha. Ngati kuli kusolola, asolola basi ndipo amaliza. Tsopano ndi nthawi ya Kongeresi. A Sidik Mia amene analowa chipani cha Kongeresi auza anthu a DPP kuti alongeze katundu wawo mmboma chifukwa 2019 kulibe… ...