
Apolisi aphulitsa utsi okhetsa misonzi ku Ndirande
Anthu okhala ku dera la Ndirande mu nzinda wa Blantyre ali wefuwefu kusaka madzi odzithira ku nkhope pomwe apolisi akuphulitsa utsi okhetsa misozi ku makomo kwa anthu. Anthu ena adandaulira apolisi kuti ayesetse kupeza njira… ...