![](https://malawi24.com/wp-content/uploads/2022/03/Dan-Lu-6-235x176.jpg)
‘Tulani pansi’ – Dan Lu wauza Chakwera
Katswiri oyimba nyimbo zachamba cha afro pop, Dan Lufani, yemwe amadziwika ndi dzina loti Dan Lu wauza mtsogoleri wa dziko lino a Lazarus Chakwera kuti alephera kulamulira ndipo atule pansi udindo. Izi ndi malingana ndi… ...