
Namondwe Jude wafika ndi chifunga komanso mvula yowaza mu mzinda wa Blantyre
M'mawa wa tsiku la lero pa 10 March, 2025, dzuwa silinaoneke mu mzinda wa Blantyre, mvula yowaza ikugwa pakadali pano ndipo ndi yomwe yakuta mzindawu. Kudzera ku nthambi ya boma yowona za ngozi zogwa mwadzidzidzi… ...