Chakwera lero akuyendera Tropha Estate, Kwithu Kitchen
Pomwe akupitilira kuyendera zinthu zosiyanasiyana mchigawo cha ku mpoto, mtsogoleri wa dziko lino a Lazarus Chakwera, lero ali m’boma la Mzimba komwe akuyendera Tropha Estate ndipo akatelo apita ku Mzuzu kukayendera malo ophikira zinthu zosiyanasiyana… ...