Sitima iyambiraso kuyenda pakati pa Lilongwe ndi Blantyre
Anthu oyenda maulendo a pakati pa Lilongwe ndi Blantyre tsopano adzikhala ndi chisankho cha mayendedwe awo pomwe boma lalengeza kuti maulendo a sitima yapamtunda ayambiraso pakati pa mizinda iwiriyi. Izi ndi malingana ndi nduna yowona… ...