Kalindo ampeza osalakwa

Omenyera ufulu Bon Kalindo, wayamba kuchotsera milandu yomwe akuzengedwa pomwe khothi ku Zomba lalamura kuti nkuluyu ndi mfulu pa mlandu oyambitsa zipolowe omwe amazengedwa m’bomalo.  A Kalindo omweso amatchuka ndi dzina lawo la pazisudzo la… ...