
Kwelepeta adandaulira Nyumba ya Malamulo za kuchedwa kuwathandiza pa kusweka kwa galimoto lawo
Aphungu ochuluka achizimayi ndi ena aamuna Lero atuluka mnyumba ya Malamulo kuwonetsa mkwiyo wawo pomwe ati Nyumba ya Malamulo sikuwathandiza a Grace Kwelepeta omwe ndi phungu wa dela la Zomba Malosa ndipo galimoto lawo linabowoledwa… ...