Mikango yachuluka, ikufunika njira zakulera – yatelo African Parks
Bungwe la akatswiri owona za kasamalilidwe ka nyama zakutchire la African Parks lati likufuna lipemphe boma la Malawi kuti liyambe kugwiritsa ntchito ndondomeko ‘yakulera' pa mikango ponena kuti yayamba kuchulukana kwambiri maka mu nkhalango yotetezedwa… ...