Achinyamata 140 akupita ku Israel mawa
Achinyamata okwana 140 akuyembekezeka kunyamuka m'dziko muno mawa kupita ku Israel komwe akukagwira ntchito ku minda. Achinyamatawa omwe afika kale Ku Kamuzu International Airport akhala akunyamuka m'bandakucha wa lachitatu. Polankhula ndi Malawi24, mkulu wa kampani… ...