Chakwera ndi samva mnkunkhu – Chatinkha
Mmodzi mwa anthu odziwika bwino otsatira chipani chotsutsa cha Malawi Congress (MCP) Mai Chatinkha Chidzanja Nkhoma adzudzula mtsogoleri wa chipanichi kuti mdiosamva za amzake. Mai Chidzanja Nkhoma ati kusamva kwa mtsogoleri wawoyo a Lazarus Chakwera… ...