Chakwera walamula lipoti la ngozi ya ndege lipelekedwe ku maanja
Mtsogoleri wa dziko lino a Lazarus Chakwera ati lipoti la zotsatira za kafukufuku wa ngozi ya ndege lipelekedwe kwa maanja okhudzidwa pofika lero Lachisanu. A Chakwera atinso kuyambira lolemba lipotili alitanthauzire mu zilankhulo zina za… ...