Mulili wa chikuku wabuka m’boma la Mchinji
Unduna wa za umoyo wati m’boma la Mchinji mwagwa muliri wa matenda a chikuku omwe pano agwira anthu asanu ndi awiri (7) m'bomali. Malingana ndi kalata yomwe wasayinira ndi mkulu wa zaumoyo m’bomali, Dr Yohane… ...