Ophunzira a MUBAS akusonkhetsa thandizo la ophunzira mzawo emwe akufunikira thandizo
Awa mukuwaona pa chinthunzipa ndi ophunzira apa sukulu ya ukachenjede ya Malawi University of Business and Applied Science (MUBAS) mu nzinda wa Blantyre ndipo iwowa akonza mwambo otolera thandizo loti lithandizire ophunzira nzawo amene akudwala… ...