Mfumu ya zinyau ipereka mphatso kwa oyikonda
Mu nyengo yino yachisangalalo yimene kumakhala zikondwelero za masiku a Khirisimisi ndi Nyuwele, mfumu ya zi Nyau sinalore kuasiyasiya oyikonda powapasa mphatso. Mfumuyi imene dzina lake lili Limbani Kalilani, yapereka phukusi la nyimbo zisanu ndi… ...