
Bungwe la Southern Region Water Board (SRWB) yati ili ndi chikonzero chomanga dam lalikulu ku Domasi m'boma la Zomba limene lithandizire kuonjezera madzi amene bhodiyi imagawa komanso kuthandizira pa ulimi wa mthilira, ulimi wa nsomba… ...