
Tsogoleri wa mpingo wa Chikatolika pa dziko lonse lapansi Papa Francis lero waonekera ndi kupereka moni ku khwimbi la anthu limene linasonkhana panja pa chipatala atagonekedwa kwa ma sabata asanu m'chipatalachi. Malinga ndi nyumba zofalitsa… ...