Nzika za ku Malawi zokwana 300 zomwe zimakhala m’dziko la South Africa koma opanda zikalata zokwanira azitumiza kuno kumudzi. Potsimikiza za nkhaniyi, wachiwiri kwa m’neneli wa nthambi ya boma yowona zotuluka ndi kulowa a Wellington… ...
Articles By Mphatso Khutcha Richard
Osewera mpira wa miyendo yemwe ndi m'modzi mwa a chiyamba-kale m’dziko muno, Joseph Kamwendo wati iye akukula koma mu maseweredwe ake a mpira ma timu adziwaphera nzeru. Kamwendo yemwe pakali pano akusewera mpira wake mu… ...
As the health sector in the country continues to encounter drug pilferage, Machinga police are keeping behind bars two Health Surveillance Assistants (HSAs) for stealing drugs. Machinga police spokesperson Davie Sulumba identified the suspects as… ...
Be Forward Wanderers have warned their fellow Airtel Top 8 chasers that they should not count on the injuries of Lucky Malata and Francis Mlimbika as a chance for them to easily pass through. Nomads… ...
A 40-year-old man who raped his 16-year-old daughter in Machinga district has been sentenced to 12 years in jail. The rapist, Kanyenga Damson, was found guilty of defilement which is in conflict with section 138… ...
Munthu wa umunthu amakhala ndi chisoni, mantha, ulemu mwa zina koma izi sizili choncho m'dziko muno pamene mchitidwe ophana ukupitilira. Izi zikutsimikizika pamene bambo wina wa zaka 67 ku Nkhatabay wapezeka ataphedwa ndikudulidwa mutu komanso… ...
Pamene masewera a chikho cha ma timu asanu ndi atatu mu chikho cha Airtel chomwe chifumbire kuyambira lowelukali, anthu ena otsata za masewera a mpira wa miyendo ati chikhochi chikhalangati ngati kukumba madzi pa thathwe… ...