Mtsogoleri wa aphungu otsutsa boma ku Nyumba ya Malamulo a George Chaponda ati zomwe achita apolisi komanso anthu ena omwe alepheletsa ziwonetselo mu nzinda wa Lilongwe ndi m'chitidwe okupha ufulu wa nzika za dziko lino.… ...
Articles By Mphatso Khutcha Richard
Timu ya mizilazembe yomwe ikutsogolera 2024 TNM Super League m'dziko muno ya Silver Strikers kudzera kwa m'phunzitsi wake Peter Mponda yati timu ya Bullets singabwere pa khomo pawo kuti idzawononge mbiri yawo ya kusagonja chiyambileni… ...
Wachiwiri kwa mtsogoleri wadziko lino a Michael Usi awuza anthu amene anasonkhana pa nsika wa Lunzu m'boma la Blantyre kuti asamangokuwa za kusowa kwa mafuta koma adzifunsa kuti zina zikuchitika chifukwa chani ndi pamene adzakhale… ...
Atachita ma pulakatesi panja pa Radisson Blue hotel kukonzekera masewelo mu 2025 AFCON Qualifier ndi Burundi pa bwalo la Felix Houphouet Boigny in Abidjan, mdziko la Ivory Coast, lero Malawi yapatapo point yake yoyamba chiyambireni… ...
Ukali wa Silver Strikers chaka chino wawonekanso usiku wa loweluka pa masewelo a mu ndime ya ma Timu anayi ya mu Airtel Top8 pa bwalo la Bingu mu nzinda wa Lilongwe pamene yaswa mtima wa… ...
Usiku wathawu, monga zikukhalira ku Malawi, mizere masiku osowa mafuta ano, azibambo anatsala pang'ono kutsilana makofi pa malo omwetsela mafuta a Tengani Engen m'boma la Nsanje, pamene panalowa chisokonezo pa mizele ya anthu omwe anandandana… ...
Atakanika kugonjetsa adani awo a mu Lilongwe, mphunzitsi wa Silver Strikers Peter Mponda wati kugonja ndi Civil service United ndi zokhumudwitsa. Anyamata a ma Banker omwe anayitana anyamata a Civil pa bwalo la Silver mu… ...