
Apolisi ku Lilongwe amanga banja lina lomwe akuliganizira kuti linaba khanda la masiku awiri pa chipatala chachikulu cha Kamuzu. Malinga ndi Mneneri wa polisi ku Lilongwe a Hastings Chigalu, a Wyson komanso Gloria Misoya, onse… ...