Ngati a Peter Mutharika amayesa kuti akadutsa moyela ku convention yawo, apa ndiye aganize kawiri. A Kondwani Nankhumwa sali mocheza ndipo ati akawaswa a Mutharika. Malinga ndi wailesi ya Zodiak, a Nankhumwa ati iwo sabwelera… ...
Articles By Mike J. Kangwele
Mukamva ena akupitirira kunena kuti agona pa filling station chifukwa amasaka mafuta, adziweni ndi opanda chilungamo chabe. Mafuta analonjezedwa kufika lero aja tsopano afika. Ngambwi ngambwi, a Chakwera sakucheza. Patatha sabata a Malawi atazunzika ndi… ...
Mizere yonse mukuyionayi, ati mukuyiona komaliza. Kuyambira lolemba lomweli ili, mafuta akhala paliponse moti malo omwetsera mafuta azichita kuyitanira anthu. Atelo ndi a boma. Malinga ndi mlangizi wa a Chakwera a Ephraim Chibvunde, mafuta osowa… ...
Olira samugwira pakamwa ndipo mneneri wakale wa chipani chotsutsa cha DPP, a Nicholas Dausi, walira mokweza pa mwambo wa maliro wa a John Tembo. Poyankhula pa bwalo la za masewero la Dedza pamene amaimilira anzawo… ...
…Bullets yakanika kuzemba pa Mazembe Zikakhala nyerere zikuti ndi chifukwa kunalibe ma ref ogulitsa, eni ake a Bullets ati bola anafikako ku CAF. Koma lero pa 30 Sepitemba ulendo wa Bullets watha basi. Mazembe ya… ...
Kapena mwina a Malawi tasukutsula mmaso pa njuga mpaka takhaulitsa mzungu? Koma a kampani ya Premier Bet ati vuto ndi chuma. Ndipo tsopano ayamba kutuluka msika wa ku Malawi. Awo paulendo kutsatira DSTV. Kampani yotchuka… ...
Ati mukamva za anthu osowa, kenako kuzindikira kuti aphedwa, muzingokhala chete basi ndi kumati Chakwera 2025 boma. Ati kufalitsa nkhani za kusowa kwa chitetezo mu dziko muno mutha kupezeka nazo ku jele. Atero ndi a… ...