Malawi hit with fuel crisis
Mukamva ena akupitirira kunena kuti agona pa filling station chifukwa amasaka mafuta, adziweni ndi opanda chilungamo chabe. Mafuta analonjezedwa kufika lero aja tsopano afika. Ngambwi ngambwi, a Chakwera sakucheza. Patatha sabata a Malawi atazunzika ndi… ...