Kulira komwe kukuganizilidwa kut ndikuwombera kwa mfuti kunamveka pa msonkhano wa a Donald Trump ku dera la Pennsylvania pomwe mtsogoleri wakale wa dziko la America'yu amalankhula. A Trump anachotsedwq mwa nsanga ndi akuluakulu anthambi ya… ...
Articles By Ephraim Mkali Banda
Bungwe lowona za ufulu wa anthu la Malawi Human Rights Commission (MHRC) lati makolo a mwana wa sabata zisanu ndi ziwiri yemwe anamwalira pa chipikisheni cha Mtambalika (road block) m’boma la Mzimba mwezi wa June… ...
Yemwe anali katakwe womwetsa zigoli mu timu ya mpira ya dziko lino Kinnah Phiri wauza Malawi24 kuti timu ya Flames ingakwanitse kupita ku AFCON pamaso pa Senegal komanso Burkina Faso, omwe ali mu Gulu L.… ...
Minister of Lands Deus Gumba says the government will construct more houses for people living with albinism to ensure they are living in a safe and secure environment, as promised by President Lazarus Chakwera. Gumba… ...
Wolankhulira Polisi ya Balaka, Gladson M'pumpha watsimikizira nyumba zowulutsa mawu m’dziko muno kuti anthu enanso awiri amangidwa m'mamawa wa Lamulungu kutsatira nkhani yokhudzana ndi mayi Matako omwe anawanjata dzulo chifukwa chozunza mwana wawo wamkazi atampeza… ...
In a remarkable act of philanthropy, an American citizen, Linda Anne Ward, has spearheaded the renovation of Kamteteka Health Centre in the Mzimba district. The facility, originally constructed in 1984, had fallen into disrepair over… ...
Police in Mzimba district have arrested four people for allegedly being involved in illegal mining at Chikosera village in the area of Traditional Authority Chindi in the district. Mzimba Police Station deputy public relations officer… ...