Bungwe la Ulama Council of Malawi lapempha mabungwe omenyera ufulu wachibadwidwe, atsogoleri a ndale, komanso atsogoleri azipembedzo kuti adzudzule zomwe boma la Malawi likuchita pa nkhani yolimbikitsa dziko la Israel kupha mtundu wa Mapalestina. Polankhula… ...
Articles By Ephraim Mkali Banda
MISA Malawi has launched a two-day workshop in Mzuzu aimed at bolstering investigative journalism skills among community radio broadcasters in Malawi's Northern Region. The training, attended by 30 journalists from various community radio stations, is… ...
Akatswiri a za umoyo dera la kum'mwera kwa boma la Mzimba ati chiwengero cha achinyamata omwe akutenga matenda opatsirana pogonana chikunka nakwera tsiku ndi tsiku. Malingana ndi yemwe akuyang'anira zamatenda opatsirana pogonana pa chipatala cha… ...
It has been established that Rumphi District is one of the potential districts in the country that can do well in tourism and bring foreign currency to the country, including job opportunities for Malawians. The… ...
Katswiri pa nkhani za ndale, Thomas Chirwa, yemwenso ndi mphunzitsi pa sukulu ya ukachenjede ya (University of Dar Es Salaam) koma ndi M'malawi wati ndipovuta kuti andale azipani zotsutsa asiye kumayankhula za imfa ya yemwe… ...
Mtsogoleri wa dziko lino a Lazarus Chakwera watsimikizira bungwe la International Monetary Fund (IMF) ndi World Bank kuti dziko la Malawi lipitiliza kuika njira zabwino zokwezera chuma chake. Chakwera wanena izi pa mkumano ndi akuluakulu… ...
Timu ya mpira wa manja ya Mzimba Queens yakhala akatswiri a Salima Sugar Netball Tournament chigawo cha kumwera kwa boma la Mzimba. Timu Mzimba Queens yathambitsa timu ya Raiply Queens ndi mitanga yokwana 56 -… ...