Mtsogoleri wa dziko lino a Lazarus Chakwera, apemphedwa ndi Bungwe lotchedwa Public Affairs Committee (PAC) kuti achepetse nduna zake komanso chiwerengero cha azilangi ake ndicholinga chofuna kupulumutsa chuma pamene dziko lino lakutidwa ndi mavuto osiyanasiyana… ...
Articles By Ben Bongololo
Mayi wina wa zaka 24 zakubadwa m'boma la Nkhotakota watsekeledwa mchitokosi pa polisi ya Nkhunga kamba konyoza ndikutukwana apolisi kudzera pa tsamba lake la mchezo la Fesibuku. Mayiyu yemwe dzina lake ndi Anastasia Kamanga, adatukwakwana… ...
Anthu atatu m'boma la Dowa alamulidwa kuti apereke ndalama zokwana K2.7 million aliyense kapena kukaseweza ndende kwa miyezi yokwana makumi atatu (30) atapezeka olakwa pa mlandu opezeka ndi chamba. Anthu atatuwa omwe ndi a Charles… ...
A Martha Chizuma omwe ndi mkulu wabungwe lothana ndi katangale la Anti-Corruption Bureau (ACB) ati utsogoleri wa a Lazarus Chakwera waonetsa chidwi chothana ndi katangale m'dziko la Malawi. Mkulu wabungweli amayankhula izi ku nkumano omwe… ...
As a way of supporting farmers, Bilal Trust- Central Region has distributed bags of fertilizer and seed packs to 1800 people in over 28 villages in Nkhotakota district. Malingana ndi zomwe walemba Kanyenda pa tsamba… ...
A Bon Kalindo omwe amachititsa zionetsero lero mu mzinda wa Blantyre apempha boma kuti likweze malipiro a anthu ogwira ntchito m’boma ndi K50 pa K100 iliyonse. A Kalindo, ati ndichitonzo kukweza malipiro a ogwira ntchito… ...
Patricia Kaliati yemwe ndi mlembi wamkulu wa chipani cha UTM wauza a Malawi kuti akuyenera kuyika maso komanso chiyembekezo pa a Saulos Chilima yemwe ndi mtsogoleri wachipanichi. A Kaliati amayankhula izi dzulo m'boma la Kasungu… ...