Mzuzu University student, Natasha Rashid has advocated for the legalization of abortion in Malawi, citing the reality that despite its illegality, women continue to undergo unsafe abortions in secret, putting their lives and health at… ...
Articles By Ben Bongololo
Bambo wina wazaka 42, ku Lilongwe wakadzipereka yekha m'manja mwa apolisi ku Area 3, atakhapa ndi kupha mkazi wake ndi nkhwangwa atazindikira kuti mkaziyo akuzemberana ndi njonda ina. Mneneli wa apolisi ku Lilongwe, a Hastings… ...
Mzuzu University's Face-to-Face Student Association (FAFASA) is spearheading a fundraising initiative to support fellow students facing financial hardships amid a rising number of students struggling to make ends meet, particularly those not benefiting from the… ...
Apolisi m'boma la Salima, amanga bambo wina wazaka 31 zakubadwa yemwe dzina lake ndi Mathews Daimon, kamba komuganizira kuti amasunga mankhwala achipatala osiyanasiyana popanda chilolezo mnyumba mwake. M'neneli wa apolisi m’bomali, Sub Inspector Rabecca Ndiwate,… ...
Awa mukuwaona pa chinthunzipa ndi ophunzira apa sukulu ya ukachenjede ya Malawi University of Business and Applied Science (MUBAS) mu nzinda wa Blantyre ndipo iwowa akonza mwambo otolera thandizo loti lithandizire ophunzira nzawo amene akudwala… ...
Two Mzuzu University graduates, identified as Harriet Nkhoma (33), Wongani Nsona (28) and a 3-year-old child, have lost their lives in a road accident that occurred in the early hours of Saturday at Chimbiya Trading… ...
Fomo yaluza womwetamweta pamene yalepherana ndi anyamata a Mighty Tigers. Fomo inapeza chigoli choyamba pa mphindi khumi ndi imodzi kudzera mwa osewera Hassan Hussein. Pamene zimakwana mphindi makumi awiri ndi ziwiri (22) naye osewera wa… ...