Patsepatse nkulanda. Kupalamula ndi konse ndithu koma milandu inayi ndendende kugenda ku Polisi wamkulu fodya ali mthumba.
Bambo wina wa zaka makumi awiri ndi mphambu zisanu kudza imodzi (26) ali m’manja mwa a Polisi atagwidwa pamene amafuna kutsomphola phasulo m’manja mwa Mtsogoleri wa dziko lino a Peter Mutharika.
A Bambo Francis Itende ati anachita chipongwe chawochi pa 23 December chaka chatha pa Songani mu boma la Zomba.
Ati a Mutharika anayima pa malowa kuti agawile kangachepe kwa amayi a chipani chawo cha DPP amene amawayimbila nyimbo.
Apa Bambo Itende anaonapo mwayi oti atsanzikane ndi umphawi.
Ndiye pamene a Mutharika amafika, iwo basi tsompho! kulanda phasulo lomwe a Mutharika adanyamula.
Iwo sanapite patali ndi upandu wawo ndipo a chitetezo cha a Mutharika adawambwandila.
A Itende amene amachokela ku Dedza akuyembekezeka kukalowa mu Khoti.
Maluzi aonjeza pa Malawi sanalakwe munthu
Naye Gwaladi anyanya kugawa makobili.Don’t he know kt this is Tantamount to February??? Ma envelope mbwe ngat amagwila ganyu Post Offece.Anafunaka mukumulanda evelopyo nd kumutibulaso Makofi athazi angazaname
Olo ndili ine ndimasomphola mkupotokola mkono
Mwachita bwino akawone mavuto
Mauwa alembedwa kt anjatiwa, so where is de mistake????
Umphawi kumalawi
Zangoonesa kt amalawi tili mmavuto azachuma
Kkkkkkk koma Ku Malawi iiii zinaukanva
Koma Peter Ndi chitsilu cause munthu amafuna kumupatsa ulemu kumunamizira kut akufuna kumubera 2019 peter usawuka coz mitsokho sutegaso ufalika chitsilu
Dr Peter masulani munthuyo mvesan kt kumalaw ndalama yafika povuta moti kumanga masikiniyi nkungoonjezela mkwiyo wamizimu
Nanga adzidya okha zakubazo
Angomukhululukira ameneyu, sadzachitanso. Kumashondokola apresdent ndithu, koma ameneyu! Nawonso apresdent,… Mmmmmh.
Bola Watchuka Dziko Lonse. Kuti Ndimunthu Oyamba Kulimba Mtima Kukafika Pafupi Osaopa Ma Boardguard Kk 2018 Zayamba Bwino
Kkkkk ameneyo Ali gulu LA anthu amene amatizunguza kupulaimale ndithu kkkk mpaka wakatsompholaso President kkkk achitetezo anali kokamwa matokoso eit?kkkk
Chonde mwanayo musamupange tintini ndiwosalakwa vuto ndi achitetezo alephela ntchito yawo.apresdent pamenepo adziwe kuti alibe security kodi pamenepa mwanayo akanakhala kuti anatenga bomba sibasi apatu gwape anafatu.
Kkkkkkkkkkk koma ndie ndi letest2
Anyanya ma handouts envelops paliponse chilungamo sichigudwa
Kkkk anamusomphola chani kodi ndalama?
Amafuna misokho yake muthu mukufuna muzingodya nokha
Mwana wankhuku aonela make kunyera m’nyumba, ndiye anjatwa ayeranso kuhasula
akulanda mbava izake
Kufuna kudzipatsa yekha pension yake kumeneko kkkkkk
Where was body guards? And why are you publishing this because you are jeopardising president security. Bodyguards need more training of escorting VIP. This is embarrassment. Why did they give home a chance to come close? Eish koma Malawi
Anjatwa ndi mau onyazitsa kuchichewa amatero
Mmm gyz ine ndnalipopo, nkhan ndyoti adawa analezela ndye amafuna kumugwra zanja presedent pamene amaweva mfanz. By dat tym mmanja mwa peter mudalibem kath.
Asamunjate wawonetsa luso ameneyi ndi shasha
Cadet kutopa ndikuzola paint naye amangoyenda ndi envilop mmanja amafuna akampase ndani
Ine zakubazo ayi, koma ndati ndi gonenako pa amene mumakhala busy kumachonga zomwe anzanu alemba. Nthawi zina ndibwino kukhala chete ngati ulibe zonena. Meachitsanzo; ena mukuseka mau akuti anjatwa, ine ndikutsimikizireni kuti amene walemba mau awa ku school adapitako. Ndipo school yake yaukachenjede. Ambiri timalimba chichewa kapena chingerezi cholakwika. Kwa amene akuona ngati liwu lakuti anjatwa ndilolakwika, ameneyo alitenso nkalasi ya Chichewa ndipo akaphunzire phunziro la mau onyazitsa. Kumeneko akapeza mau ngati amenewa, kungoonjezapo akapezaso mau ngati pezwa, mangwa, pangwa, menywa, etc. Ndiye chonde tiyeni tizingowerenga ndikunva chomwe chikukambidwa kusiyana ndikumakhalira kuchonga zolemba ena. What one doesn’t know doesn’t exist. Ndangodutsa
Ena amayiwalanso kuti pano pamapezeka anthu a xul zosiyana, pamene ukudzimva kt udafkapo mnzako wina imeneyo ndi form 1
uli bo ayise, ndiwe brains, chichewa language umachiyazadi.
Anjatiwa
Kodi mukuti chani pankhani imeneyi chachitika ndichani admn
Amasudwe anjwatayo vuto siiye koma mabodygard odotha kapena ombwambwana siyeni
Kupusa kwaboma muthu ameneyo gofunika kumulemba ntchito akhale bd guard wa prdnt ooo cz waonesa udolo anakafuna kupha anakapha
Mbava ndi ma cadet
Achitetezo anali kuti
TamusiYani Munthu,ndekt penapake ndalama sikupezeka paMalawi,amafuna kt akuziwitsen Munthuyo aPresident kkk
koma please achitetezo munalikuti???
Siachitetezo onse amene akukondwa ndi zochita za APM ,nkhondo ndi anansi kkkk !
Nde mpaka kumangoonerera wina akushondokola envelope ya apresdent… Mmmmmh.
#mneni_wonyanzitsa…
Amafuna kutenga theka la chuma chake kkk
amafuna kumudziwitsa peter kut chitetezo mulibe mdziko muno komanso maluzi avuta kwambiri.nanga ngat akubeledwa mtsogoleri wa dziko kulibwanji nzika za mdzikomo.am not from mcp or pp but am a citizen of the republic of MALAWI.
Next time tizanva kut amuba, nanga security yake imene ija munthu nkusomphola ndala mmanja ma president alinso mgalimoto?? Haha ndikanakhal ine ndikapanga za sacking bas alephela pa ntchito yao ya chitetezo.
kkkkkk awonjezadi achitetezo ake, mpaka kusopholedwa.
komanso president safunika kugawa pamanja akadawapasira antchito akeeee
kkkkk atani?? anjatwa ndekuti chani admn muzisuta chozimisila
Vuto losekerera ma Cadet ndi limenelo. Ngati mumawasekerera kuti azimenya a police as they did pa Tsangano. Here it is now. They don’t fear even the State President security. Mwana wokulira pa chilolo…………. Musamulange ndi wanu mudamuzoloweza kale. Vuto si iyeyo, mixxx
kumanga munthu osalakwa pomwe MUTHALIKAYO tsiku ndi tsiku akuba misonkho ya amalawi? kumeneku ndikulakwa.MOTI M’LANDU WA CHAPONDA NDI UWUWU waukulu ndi ut?
Mbala kugwilana amatero??
Koma anthu Ena amalimba mtima kutsanzikana ndi umphawi uku?
Anjatwa yemweyo admin
kodi mwayamba kulemba language yanji ? kkkkkkk
Admin uyu anapita ku school. Chichewa chimenechi ndichonveka kwambiri.
hahahaha! admin xul ziyamba mawa kayambeninso plizz
Chichewa 100% correct
Chichewa chonveka kwambiri kwa ife a Malawi osati Asenanu ayi.
Kkkkkkk iwe galu eti
Iyayi, sigalu, nanga si akudabwa kuti inu Chichewachi mwachidabwa, misintho ya aneni simukuyidziwa inu, nchifukwa akukunenani ka, kapena akanati Angerezi inu?! Adm, walemba zomveka kwambiri, 2pts… Mmmmmh.
Anjatwa yemweyo admin
Kkkkkkkkkkk
Mxiiim