Mankhwala a nyerere adziwika tsopano, ndi fodya wa Nyasa.
Nyerere za manoma zachoka pa Bingu National Stadium zikulila chokweza, a neba awo a Bullets atawatibula masana dzuwa likuswa mtengo.
Pa masewero amene anakodola khamu, nyerere ndizo zimaoneka ngati zipambana potengela kuti chaka chino zawo mu ligi zikukhala ngati zasongola. Malinga ndi kuvutika kwa Bullets, ambiri amakhulupirira kuti pokutha pa tsiku, nyerere zikhalanso zikumwa wa mkaka.
Koma timu ya fuko ya Bullets yangotsimikiza mbiri yoyambila 2012 yoti zivute zitani koma ku ligi, nyerere ndi akazi awo basi.
A Bullets anaoneka a njala yofuna chigoli ndipo njala yawo inaphelezela mu chigawo choyamba chomwe pamene mnyamata wawo Emmanuel Zoya anamalizitsa mpira ochokera kwa Chiukepo Msowoya kuti ukagwedeze ukonde.
Chinali chigoli choyamba cha masewelowo ndipo chotsiriza chinalinso chomwecho.
Manoma anayesela umu ndi umu kuti agoletse koma popanda zawo zokodzela pagolo zija, mpira unakanika kuthela mu ukonde. Ngakhale anasintha osewela ena, palibe chime
chimene anapindula.
Pokutha pa masewero, Bullets inali ikuyimba olire olire pamene nyerere zinali zikulila.
Padakali pano, Bullets ndi nyerere akusiyana ndi ma pointi seveni basi.
mmmmmmm anthu amanoma tiyeni tiziyamika ndi kulankhula chilungamo pa zomwe zachitika eeeee basi kungakhalila nsanje basi ,sanje siyimanga mudzi mmmmmmmm
Muli Ndi Mbali Eti? Ndiye Mukhale Bullets 24 Not Malawi Poor Reporting.
Mbuzi iwe wasowa zokamba eti osakamba za ma points bwanji kuti tili patsogoro????
Tavidzutsa vimagona va BiBi/manyi.
nyerele sizidzatheka kuzimenya koma osachokabe pachiongolero
nyerele sizidzatheka kuzimenya koma osachokabe pachiongolero
Kkkkkkkkkkkk koma nyelele
Lkkkkkkkkk koma guys adim waganizabwanj iwe ukufuna azikhweze ako?
Tiphe nyelele basi
Mkaid akadyera nyama tsiku limenelo sizikutanthauza kut watuluka, ndie neba pamodz nd wa 24 mzakoyo musandinyase if u r clever just jamp de remainin 7 steps en get me here.
Okoza pagolo uja tinamuika loko palisani,tiye nazoni Mapale zikukoma kwabax.
Usanvutike ulibe pa number 5
zaziiiii mwayamba lero kuwina ??? manyazi bwaa .jast gundi???
nyelere azifafatha kooopya kkkk bullets ikubwera komweko
Hahaha neba mutu sukugwira
Kumapanga pangabe ma comment kuti Neba azipsa mtima
mwakhala ngati mwadyera nsima yanyama mziwona mtsogolomu palibe chanu chakachino
Big up NYBB fc!!! ye’ did a great job beatin’ up so called nyerere, they’re rude and talkative before action yet they’re not super league winning material.
T doezn’t mata kt kaa mukt muli pa top kaa wat?kma nkhan ndyakt BB yakuthizimulan…ngt muli pa top nanga ku Bingu mumakatan osangokhala pot mukt league mudatenga kale?mukat team yathu ndyambuli mufuna munene kt cha?ku Noma ophunzra ndan?JC ndi wa std 3 kkkkk,JK Fm 2…ndsachte kupitiriza mundibasope!BB yayaka moto,inu mukawina simukondwa?vuto laku Malawi anthu jelous bac mmmm Neba vomereza
Mphaka wabibira mudengu LA UFA wa manoma
Zozizila za fridge nyasa yo yaluza kangati pa Bingupo????? A bullets muli ndivuto mukawinako.
Akalawako kachigoli
Akufuna ativute pot kuwina ndi nkhani yachilendo azathuwa kkkkkk.
kkkkk.kulemba nkhani moseketsa uku.kkkkkk
Ana a mwano kulandira mphoto yawo nde tsoka poti nayo silver strikers mkwiyo wawo komanso wa mzuni ukutsikira komweko mulira chokweza aphwanga
Wakutumayo akupwetekesa, #nyerere4life
ndiwe Chitsiru admin mesa ndi mmene umakhalira mpira kodi mesa nomaso imawapambadza some other time ngakhale zili choncho koma nyerere zili pa top
Kod a m24 ndnu a chngabwe fc? Pa…panu
Takunyenyanibeni.
ii kaya ine nde sindikunena nawo….zongofuna kudanitsana basi kkkkkkk eti my swthat Tryness Chikumbutso Msosa
Mani ine fra mapare ndi mapare
koma iwe ndi mtolankhanidi?sindinaone ntola nkhani atalemba zinthu mopanda nzeru chonchi
some reporter’s are worse than dogs
Eeeee Malawi 24 mwatiimililadi mankhwala a nyelele apezekadi ngakhale atukwane
ABB ulemu mulibe mukawina ndi mwana yemwe ama ziwilatu kuti BiBi iyoo akoza ndi a bibi kkkkkkkk
kodi ndiinu ateam yanji
Kkkkkl koma admin ati popanda zawo zija zokozela golo
Ukazolowe kuyenda mapazi opanda nsapato ukagula gondola umayesesa township yonse iyiwone ndithu gondola
Izi nde zobeba nyerere zmavta kzthesa kwake
Ndiye iwenso ndi Neba eti ? Nkhani amalemba chonchi
Chigoli cha off side-cho
Bola chili chigoli, mimba yako
Hahaha Wena Mimba yako
Still Noma # 1…league tikutenga iyi…hahahah
Nooooo!!
woooow akause muntendera.
Ngakhale tili pasi Paso koma tawapondabe nbb woyeee
Bullets Ndi Dilu Noma Sidutsa Pa Bullets Mu League Ndipo Sidzadutsaso
Admn mwaonjedza chakuti chanu uzisakhire wekha nyapapi iwe
Ukawina neba umakhala ndimakani koma uziwe kuti uli behind us.
Kkkk neba ukwekwe dzulo
pepani pepani pepani Olira malirowa tikalilira Ku BT pafupi ndi Shop rite. Ophika tikakumane Ku Chichiri S S. Mafumu tipite kumzengezi Ku BWB. Akwaya tikumane pa Clocktower.
But they still at top postion.WHAT FUNNY!
Thanx to Bullets prayers for lifting up our image,for Nyerere tiyeni tidyere limodzi poti awa ndimasewera otukulira dziko la ife
Mankhwala a NYERERE ndi zoya EMMANUEL ZOYAAAAAAAA!
Iwe Waoneselatu Kuti Umaikhumba Noma Chingabwe Chinakukwana
Bullets mankhwala ophera nyerere…
bad reporting it must b balanced not 2 hav a side lyk u hav done it only shows u are also a dpp cadet shame on u
Reporter. Ameneyo ndichisilu unthenga umafalisidwa choncho? Chisilu cha reporter
kkkkk mbuzi zama reporter
Kkkkkkkk????#mbuzi??? za ma #soilder!!!
Neba Munali Kutali Tachita Dala Kuti Musuntheko Pang’ono . Nyerere Pa Ize!!!!
Ok
Zoooopusa page yi kodi ndiya bullets eti
Koma a Malawi24 ngt ukundmva malembedwe ankhan otere akusonyezeratu kut ngatid uli nmtolankhan inali wa supplementary sukudzwa malembedwe ankhan mtolankhani samaonetsera Mbali polemba nkhani
Noma imachepela nthawi zonse sakudziwa kuti timangowasiya dala pano ndie basi nyelele zalowa kuuna kkkkkk
hahaha NEba pepa
Kkkk koma mitu ya nkhani zina inu kkk
Noma wooooyeeeeee ine wanyelele basi
Vuto ndlot maneba mumasewera wapakamwa pamene ife tmasewera paground inu mwayamba mwagonjetsa bullets mu tnm,ndpo chtengeren tnm ndlt? afis inu mmayankhla moknya mapaz ndkluza kwanko.Nawenso usadane nd M24 chfkwa chankhaniy sumanena ngat mulunguyo nd m’bale wako amene al ndmphamvu andmenye kkkkk!
munma nonse a BB
Now neba waziwano kuti mpila suwina ndi pakamwa koma ground sorry neba may be next tione
neba ukunakhala wina ukanangosia kulankhula coz,pa bingu inuyo kanali koyamba dzulo kuti winapo,,komanso ife uluza koma tkupezekaso pa #1 y ? ndinu ana mwachepa,,mwayiwala tsiku lija tnakumenyan 5;0 pa bingu pompo ?,,,,vuto neba umayiwala nsanga aaaaaaa ana mwachepa .
Ngati mukutukwana chifukwa BB yawina, kulibwanji Noma ikanawina, mukanatukwana motani ?
Vomerezani kuluza. Mwayi owina a Noma unalipo, chifukwa anasewera bwino kwambiri. Mmalo mwake mwayiwo wagwera BB.
Ndiyamikire Noma potsogola ndi ma points 7. Koma ma game adakalipo amene angathe kusintha zinthu.
Iyinso nde iti!!! MANYAKA
manyaka enienitu
Kkkkkkkkk
ndipo Noma anthu sakugona nayo tulo ndaonano
Ana achEpaaaA bullets ndi deaL
Kufa ndi neba ndichiphinjo
Kwanthawi yoyamba kukhala ndi stadium yabwinotu
tiziyamika ma china nanga amwenye
Yona Malunga (Anayo)analekeza form 2 ndpo sanalembe jc, tafufuzanso kuti, Anayo magazi awo nd a blue,ndpo ma report akut Anayo pa ukwati wawo anavala suit ya America, kkkk…suit avalira pa ukwati heh nyerere. Good morning my nebaz?
Bullets oyeee ! zakuvuta basi neba.
kagwele uko cha kampopi24
Tili Pa Top Basi, Noma Woyeeeeee
Admn umatha koma unaiwala mau amozi azifwafwantha
IIIII ANOMA MUNALARARATA KWMBR ZOMELEZANI KT ZATIVUTAH BULLETS MUZIYIPASA ULEMU KWMBR
Nkhumba fc Tazibwanyakula kkkkkoo sanakodzere pa golo
Mukalaula mumavuta paja. Titsegule mmimba xomwez?? Aaaaaaaa pitan kumwamba mene mwawinamu a BB
Kkkkkkk zafa zonse nyerere
Kkkkkk
Kkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkk…..tayimeta mpala ndi galasi
Nyerere azithira Zoya guard dust
Thanks the peoples team
Uku nkuyamba wanyerere aziona yasala ndi silver ndi moyale ipanga zomwezo! Mumadalira kamwendo eti!
Kamwendo ndiwanu? Kkkk timamudalira mensa ndiwathu
Musatero,ma player anatopa ndikubina kuukwati wa yona kkko
Noma pakana yesu azatiitane muisova nomaaa iyooooooo
kanyenda amaopa kumchitisa manyaz coz tikanakhoma china iye alimomo,kutsogola sikufika kod tnm imathera round 1?aaa watan neba
Nyrerere azithizimura azisambwaza azisosontha azifafanta yilira yithambisa
i told u guyz osamangosokosa apa mpira ndipaground
Kkkkk team ya mbuli ikawina imavutatu chonde ana anu muwatumize Ku xul mwina angadzakhale openya
Am nat afootballer fun bt i hate bullets funs coz they hav won agame amakhala ngati alandla kale chikho dats shows their stupidness… So all bullets funs u hv to knw ur vry vry vry stupid coz kuwina game it doesnt min athu asowe mtendere mmanyumbanu or mmiseu.. Dem!!
Am nat afootballer fun bt i hate bullets funs coz they hav won agame amakhala ngati alandla kale chikho dats shows their stupidness… So all bullets funs u hv to knw ur vry vry vry stupid coz kuwina game it doesnt min athu asowe mtendere mmanyumbanu or mmiseu.. Dem!!
tell dem bro they are savagez
Auzeni mokuwa chonde
Kodi enawa akawina samanyadira? inu mumafuna tigwiye? zautsilu basi.USILU UMENEO
Always kuluza mu derby kopweteka
amazikaikira akawina amaona ngat kuturo
Tsiku lakufa neba pa bingu mkodzo sutuluka
Joseph ena akawina amanyadira but in discpline way nat ltk akaidi kuti awatulusa kuti akaoneko panja lol
Forget about the past lets jst look forward
Forget about the past lets jst look forward
chokaniponi apa vuto ndikudana ndi bullets ikanawina nomayo zikanakhalaso chimozi mozi asiyeni nawo asangalale akatopa asiyaokha mbwanji mukufuna kuwapondeleza azanu
To be honest am agree with you
Ndimazoba awa aiwara kuti still more tili ndi ma points ambiri ndife amamva nafe kupweteka akaidi awa
Nyerere azichotsa chimbenene..kkkkkk
Malawi 24 ana amahule nonse
Zikalowe Kucibo Amawona Ngati B B Ndianabe Kkj
Inekumva kukoma.
kkkk ndiyeyake.
Nyerere zikangogweramo zimavuta kwambiri kkkk zimaiwaliratu kuti zangogwera kkkk mkapu ya mkakatu kkkkk uisova!!!!
Man Mwasuta? Kukamwa Ngati Kwa Kkkkkk Usawonongetse C V Yako, Ife Timakunyadini Kumatipatsa Nkhani Kum Tele Uwonongetsa C V Samala
Kkkkkk Koma Mw24 Umandfkapo
Olo unyonze wansanje iwe mbuzi vomela kuluza.Ife kumwa nkaka basi
Ikadakhala Nkhan Ya Dziko Sukadalemba Choncho Kma Poti Nd Iyi Hooo!Jelasi Bas Kuluza 2 Gamez Bas Mutilambwadze?Manyaka Inu
NDE mulipa number 1? kapena mwatenga cup matama bwaa NDE mulibe manyazitu
Sakuziwa kut ife tili pa 1 bonya pa 5 kkkkk
Icn’t stop laughing!
Nde chan?
Neba tangomvomereza kt waluza basi usayankhule zambiri. Munthu akafa wafa basi sakhalanso ndi china chili chonse mthupi mwake chimene chimakhala ndi moyo.
Akananyera pagolo akanawina
Koma ndiye mutukwana kutopa?Kodi paja Noma league inatenga liti?Accept the fact you lost 3pts today. Olo mutukwane nothing changes you lost everyone witnessed it.
Takugailani 3points yo nanga mulire mpaka liti?
Zinakuvutani basi vomerezani
Kodi odana ndi team ya fuko mulipo kaphave eti?
Tazivomelezan zakuvutan bas mwaluza or mutakhala ndi 20points kusogolo kusiyana ndi bullets mwaluzabe
noma never win Bb bcz we know all the way they are pass kkkkkkkk noma take care BB its your father an till come Jesus kkk
Kuungoneseratu kuti nawe ndi mbuli ya midoli fc. Kuchita kulemba nchonchi kuti chikhare chani? Amzanu saonesa mbali polemba za sports. Samala anthu ambiri amakuziwa ndipo amakulemekeza usaononge C V YAKO
Ingovomeleza basi bro zinachitika
Amachita Matama Lero Atha
Sorry neba
AZIONA TIPATSA MAKOMBO AMATUMBWA NHATI ADYA NYAMA
Inu a malawi 24 panyini pamanu musamaonesele mbali polemba khani
No No No No No Noma! Esh!! Noise 2 Much Why? Instead Of Collecting Yur Wrongs And Searching Medication On Cholera Wayambayo Uli Busy Kulalata Pa Chulu Kkkkk Mwina Akanalowa Bus Ipite Uja Ndi Joseph Tembo O! Sorry Kamwendo Mwina Game Mukanaphula Pepani
Ife ndiazibambo noma nd ana achchepere azzwa kulemekeza akuluakulu bb we stll kep it burng
Nyerere oyeee neba usathe mau ngakhale wawina ife tikumwa wakaka iwe ukumwabe mikozo. Ndikulemba macomment ako aziiiii……
nyerere zimamenya mpira ndipakamwa. pomwe ife a Bullets timamenya mpira pa ground.
I don’t care moti ndima ndadya no stress ngakhale idali ya masamba koma ndayimaliza odandaula ndi osewelawo ine zanga pheee oluza ndi omwewo osewerawo
Tikulamulilabe t n m kuwinakwanu ndikopandaphindu ndipo mmalalata mwayiwala tinakumenyani nyelele woyeeeeee!!!! Timayikondabe sitingasike olo mutanyozabwanji noma yomweyo!!!!!!!
Kuti wa wa waaaaaaa. Noma for life
Phokoso ndikumwako Kaye milk stout ine
Zaka 5noma sinatimenyepo muligi
CHANDETU ANACHINYA CHMOZI ALIPA BECH
I dont support any team in particular but I predicted bullets’ victory though I overestimated their ability
neba wawona zomwe anaona john chilembwe ku mandala
tatsimikiza kut amadalira mikodzo lolz
Aneba kkkkkk nomazi ikutenga chiko taonan mapoisi zigori nimapenati BB ilimazi kuyandama
Neba size ikukana,ndkayang’ana ndapz kt size yakhalamba ndye ikukufitha bhoo.kkkkk, neba ng’oooooooooo wator diso lang’ombebeeee,nde ifeyo amenewo, waona bwa!!!!
Nyerere zabwira chingambwe chopela…..kkkkkkkk
Nkhumba Dzadya Anyezi kkkkkkkkkk
Sunday yalakwaso ndi blue eagles kkkkkkkkkk uziona walter
Ati Walemba Ndi Mbudzi Olembayo Sanaluzenawo Vomerani Kuluza Kuti Mukonze Mavuto Osatimtukwane Baba
Tamuthibula Neba lero kumuzwazwada kkkkkkk
Ndee wat make sense BiBi beat wanderers does BiBi now Level Points with Nomads
The peoples team deserves a win. They had a nice display all along.. Wishing them good lucky
Tionana second rnd…….zogwerazo kmaxo inu a malawi 24 mwaonje kwambr kachigoli kamodzi kukomeza kwakeko pa FB simumaoneka mwangozambaluka frm no whr…..nyerere siphada maule mwapalamula muchimina
Hahaa???? koma 3 points amatenga ndi zigoli zingati?. Ndiye ukuti second round uzatani? Chomwe timadikila pa iwe ngati Neba ndi kutolaxo 3 points kapena kugawana basi
Bvuto lokhala ndi neba oti ndi hule ndichoncho akapana 3points amafuna anthu asowe mtendere chonsechoso ali kumbuyo kwathu koma matama thoooooo mxiiiil
Hahahahahaha #neba wakhuzumuka pano chonena chagwera mkati kkkkkkk hope kuyambira pano uziperekano ulemu kwa #mkuluwako_bullets
Zia chitin a! !!
or bullets isatenge chikho koma poswa neba pokhapa mmmmmmm ine kumva sugar hvy
4m the comments u can really tell who is who kkkk “sorrow like a sharp sword ….”
Mada fucker, what de bullshit is dis?
Azipulukutadi kuziphwanya kuzififintha,akuku anati tsiku lokufa nyani mtengo umatelela.Ana achepa
admin ndiwe chisilu!! kma tili pa top noma woyeeeee!!!!
4m the comments u can really tell who is who kkkk “sorrow like a sharp sword ….”
Kunena zoona, Neba wakoyu was too fast, ziribwino pamenepa. Kkkkkk
Tisiyeni ife abibi tikumva kukoma sayankhulaso bb
Zopusa wasowa chochita eti
Nanu anyasa ngat mwasowa zolemba pitan muzikatipula madimba uko! Kuluzako yayamba ndiNOMA? Sibwino kumaonesa mbali yomwe muli polemba nkhani.
Ya thanks guys machita mushe powatibura
Koma yaaaa pali chichewa apa azisasantha,azisosola nthenga,azithibula ,azichotsa chimbenene mmmm ndikukhulupira ulindi distinction Chichewa
hahahaha kma inu wolemba khani..!
Nyerere zachepa ndi utsi wa fodya wa Nyasa!!!
Wankaka omwewo kt wawawa
anzanufe kuwina kaya kuluza we remain ve same km inu kuwina kwa lelo lokha kuchta kukhala ngat muli pa bell out mulandu sunathe tionana kutsogoloku
Jkkkkkk give admn umodzi uwiri ubwerere
Kuwina ndikumeneko kma ali panambala yanji amenewo chingambwe ?.
Shupit news yili ndi mbudzi za chilokolo izi. Wolemba news amalemba koma M24 suzatheka ndinthu ndipo sindizasiya kukutukwana iwe chi admin chopanda nzeru iwe nkhumba or bakha opanda ulemu shupiti zako!!
Cryng Ontop Of Ur Voice Kkkkkkkkkkk
Kkkkkkkkkkk yaa neh
kodi chande anolowa akuti itenga lig amuthera matama neba kkkkkkkkkk
Kkkkk neba amuthira tsabola mmaso sakuona kkkk matama amuthera
Kikkkkk kikkkkk
Koma inu a malawi24 akumenyanitu kkkkkkkk
kkk
Lumbani Nyazgambo Mtonyo nyerere bwanji
Aliponso Wina!!!!!!! Kkkkkkk
koma mumatiopa eti! mmm ndakwiya nanu
Nyerere zoona kodi akusenzetse katundu wa eni,Neba pepa ingotula pansi mwina uone ku calsberg usachinyizike ndikusenzaku ungathyole khosi asiile a Silver ndi Bullets izi si size yako izi ,wakutsina khutu ndi mnasi ukanyozera uone zomwe adaona amzako last season ndatha ine Neba wako zikomo.
Hahahahaaaaaa what explanation I like it admin!!!! you deserve best admin of the month award uzibwelabwela!!!! from to day till next wkend Neba yake ndiyowelenga ma comment osati ku commenter akumva ululu.
Zobaa wa malawi24 nyerere zkapange kukamwaa kakasi ngati ziri nd pakamwaaa umufusee #sasamba fc kuti ali kosogoro kwa zakee ndindanii
Cryng Ontop Of Ur Voice Kkkkkkkkkk
Zochta kugoner kumandazo
Kkkkk ???? amene ali pa top azaziwika second round ikazatha #Galuiwe???!!!!!???….bwanji #sunakozeremagolo ????
Neba pa easy iweyo..usaone ngati wawina league u still got 7points behind us…it will take three more games to reach us..so take a chill pill and sleep
What else can you say?
Nothing..this is enough
Hahaha,,,wamkaka
Kkkkkk komabe neba wagwira ntchito zachifundo,kkkkkkkk,BB yabwanyakula noma dzuwa lili vuuuuuuu
Ife tinali pamaliro a George Chamangwana…we are still grieving☺
Mulira mpaka liti,,life goes on basi sizonamizira kuti mukulilabe
nkhumba tazibwanyakura dzulo
nanji kukhalanso wa chelsae eish kuchimuna maliro ku chikazi maliro kkkkkk
Inu mukawina mumatenga 3points,ife tikawina timatenga BUS
bus ndkuwonongeka
Kenako mkuikonza
Kkkkkkkkkkkkkkkkkkkk ?????????????
Bola ife tili nayotu bus yo. Anthu muli kutalitali nafe koma phokoso losayamba? Pa news achita kunena kuti manoma dominated the game. Koma sinanga mikuzi yanu munatimangayo kuti tidzingogenda papolo????? Dikirani muone ife timadalira Chauta namalenga. Lol
Ife misonzi idakali mmaso ya Chamangwana tisiyeni timadziwa kulira maliro.
Kusowa chonamizila Chamangwana ali bambo ako kodi? Kodi siinu nomwe mumati muzingowina games otsalawa pofuna kugoneka mizimu ya Chamangwana yo,kapena mumanena chamangwana wina osati wapita week yathayi? Inu tabadikilani mpikisano wina wa Bus koma mu league mmmmm mukunamilatu ndi ma season angati musakutimenya mu league,kapena tinene kuti nthawi yonseyi kunali kukuloselani minyama ya Chamangwana wanuyo? Musandilankhulitse molakwika ccta ngakhale akubanja la chamangwana ko mipingu inatha kale kale ndiye mukulilabe ngati ndani?VOMELEZANI KUTI PA TENGA NYENGO KUTI MUDZAIWINE BULLETS MU LEAGUE.
Kutenga 3 point but still on position 5, what ashame, noma pachiongolero.
nkayidi akadyera nyama sikuti watuluka ,akulu ati linda madzi aduse ndiye uziti ndadala #onceMANOMAalwaysNYERERE
nkayidi akadyera nyama sikuti watuluka ,akulu ati linda madzi aduse ndiye uziti ndadala #onceMANOMAalwaysNYERERE
Am agree with you we are on top kapena aiwala akuonangati kutimenya ife ndiyekuti atenga lingi aiwale
Ndipo abullets amamva nafe kupwetekadi ndaonera apa kusangalala ngati atenga league akuiwara kuti mapoints ambiri ndiathu asiyeni alira akamachinyidwa ndiana
munthu ukakhala kt wabweleza kalasi imodzi kwa zaka zochuluka nthawi imene wakhoza kupita kalasi ina umakhala ndichimwemwe chodzala tsaya,noma yachita dala kt muone kaliliro
Mm bodza akumenyabe kkk
Kkkkkkkk Kulira Mokwezatu Uku Kkkkkk
Kulira kwa eni mtundu,pano timve kulira kwa namfedwa
Kkkkkk #dead!
Kkkk a name bodza, dala paka 90+ 3 mins
Kutsola ndichikwama sikufika apa eni ake tilanda.
Azithira phulusa lamoto
Azitsira dum
Nyerere zathiridwa Zoya guard,, Kkkkkkkkkkkk
Mahule lero apana 3points
Kkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkk nyerere koma yaaaaah pepa neba wachepa
muhehe! Kukalanga akamba admin B-) mafana oxaxamba :v more fire Maule!!!
Wakwiya ndi mfiti
tikanabe pa top #noma 4ever
Iwe ndiye wachokera kuti!!? oky ndiwedi bullututs ndawonela status yakoyi walemba muchichewa kupangila kuti mbuli zizako za bibi zimve.cz ife tinazolowera kuti malawi24 ma status awo amakhala muchingerezi.
Kkkkkkkkkkk sizikugwilizana man. Kkkkk inu school yake yomwe mukunyadirayi ndiiti? Kkkkkk
Kkkk…. iwenso waonesa umbuli wako Coz wapanga reply Chichewa,ngat uli okutha chingelezi bwanj nawe comment yakoyo osalemba muchingelezi bwanj?
Kkkkkk following kkkk
Kkkkkkk
Loading……..
chokan nanuso chingelezi ndiye Kuti chan zankutu bas simwawelengabe
Kkkkk,,,zampila2 izi
Zabwino zomse bullets
Pepa neba
Paja yona ndiogera sukunama
Kkkk tamuuzeni chilungamo ameneyu mbuzi ya mano kusi iyi school yake iti akunyadira m’malo moti adzingoyamika kuti amakwanitsa kuwelenga chichewa english amaidziwa ndi mmene akuonekelamo si mazoba osaka mbewa ameneyu.
Noma ya kupulidwa
Kma thoxy unathoka wise coz paja bb ndiya athu osazindikila hevy hahaha shame!!!
Kma thoxy unathoka wise coz paja bb ndiya athu osazindikila hevy hahaha shame!!!
Mutuluka ukweche week yonse ino a tili pa top fc
CHOKA BOLA TANKHALILANI PAMSANAPANU
Iweyo ophunzirawe walekeranji kulemba English
kumanyadila chilankhulo chathu
Bwampini iwe!
Sanalembe in english coz bb funs they cnt understand anyting okk????
Mercielago Mercie Mercie dont pray fuck thing to my team tawina tawina
We agreed kuti u have won the game but it doesnt min poti mwawina athu ena asowe mtendere this iz nat hw we support football wamva cassim captain??? Hahahaha
ife tizikuchinyanibe mu lig
bakha amutuma ameneyo pumbwa, Namtchengwa
kulira uku
I think mbuli ndi iwe opanga comment mu Chichewa we
chilungamo kamwendo ndiyemwe ama imirira noma yalero sinali noma yomwendimaiziwa ine
kkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkk
Kkkkkkk Malawi24 makwana, nyerere azithira Shumba guard Dust
Kkkkkkkkk,neba malaya athina
Kkkkkkkk nyerere zayenda ngati achule mmalo mwa nsomba
super guard dust wa expire he hehe neba remember z seven points away from mahule
super guard dust wa expire he hehe neba remember z seven points away from mahule
Wamkulu ali pamwamba…zafodya ett
Kkkkkkkkkkkkk aaaaaliponso winaaaa timusambisensooooo Neba nde tathana nawe basi ndi fodya wokoyo kkkkkkkkkkkkkkkkkk
Oooooo neba ukodza chokweza kkkkk
zidakali pamwambabe hoo
Kkkkkkkkkkkkkkk komatu nkhani zinazi anthu akukunthani nazo
Kkkkkkkk mumaitha!!
Kkkkkk koma yeah azibabada
Ndimahule athu awa
Arsenal ndi ganyu ku BB YONSE BOOH NDAMWA CREMORA INE KKĶĶ
ayayayyayi reporting imeneyi kkkkkkkk mukufuna neba athawe Ku Malawi kuno chani lol
Nyerere zake zomwe zidatenga ma star onse kukhala awozi??? kkkkk
Kkkkk nkhalamba Kanyenda wandararazi
Koma ma report ake
Kkkkkkk opsetsa mtimatu shaa
Kkkkkkk ndipo
mbuzi ya reporter ameneyi kkkkk
Kkkkkkkk ndipo mbuzidi yeniyen
Hahahaha neba 6 ikudikira uziona
kkkkk koma abale
Kkkkkkkkkkk zooanad eeee anawa achepa
Alipo mukamba naye
Lero ndaluza konse…Chelsea and Noma mmmmm but still the blues 🙂
Your WhatsApp status says ”In a meeting’’ for the past 6 months.My friend Are you planning to sell Africa or how to dry the Indian ocean?
Yakusangalasani status ya Mposh Poizon
ndapanga copy ku Mugabe nthabwala
Mwanyabe inu anyamilandu fc mulungu akanakhala nyamilandu mhmm akadabweletsa mvura kuti mpila usamenyedwe kkkķkk
Kod guyz chande,chester &sanudi anamenya? Wafa imfa yowawa nebaaaaaa.pepaaaaaB-)B-)B-):'(:'(:'(:-S:-S:-S$200 ugulile mavembe mu nseu wa zalewawu.
Kod guyz chande,chester &sanudi anamenya? Wafa imfa yowawa nebaaaaaa.pepaaaaaB-)B-)B-):'(:'(:'(:-S:-S:-S$200 ugulile mavembe mu nseu wa zalewawu.
Chitimu kunivetsa kukoma namwanso wamkaka,neba walira
“ngakhale taluza tilibe pamwamba ife” i just heard one of nyerere supporters saying that. my friend that is a baseless point to justify yourself. mwaluza basi kuvomereza ndi kwabwino.
Kutsogola sikufika, muwafunse anzanu a Blue Eagle, Mwatenga chikwama cha eni ake pepani Neba chisoni chagwela Baja Nyele
Pasadi Katole nsanje basi ankolo
Ndiye mumaganiza kuti ife sitizaluza. Nyerere for better and for worsse
Zathekabwanji sikumva
Manoma zativuta basi ife pa maule mu league ndi apogozi ndipo wothesa banja ili sindikumuwona since 2012 up tu nw zosaenda banja ili layala phasa zedi.
Neba amuumbuza,neba amufwafwatha,neba amumeta mpala,neba ampaka chtedze pa dazi,neba amathawir kuuna amkokako,neba ubongo waphulika chfkwa amaganiza zthu zot cznatheka ndpo cznatheke ndpo czzatheka,neba ubongo ukuoneker,neba bola iwe zako zilibwno ulmbkile
mukunama ndi bb 0 n noma 1
Sorry NEBA umaenda motumbwa lelo waziwona
Bola Pompo maule tkumwa wankaka gadgah.
mukunama its bullets 0 n noma 1
Neba wamwa mkodzo lero osakaniza ndi mafuta a Nkhumba
Tube Chopopa yekha Kanji Chingakanike kuphwetsa kkkk Nyerere zaona mbwadza
WE HAVE WIN WINNER
Ana onse apereka ulemu kuti zoonadi Big Bullets imatha, in the history of super league noma sinachinyeko BB.
Zangochitika koma ndimaikonabe team yanga nyerere woyeee chifukwa awa kwa relo lokha neba koma tilipasogolobe.
Ndiposo ife mtili duuuu pa top hiyaaaa
neba wasogola ndchikwama eni ulendo akubwera kkkk maule sazatheka!
noma ivomele kuti yafa
Napepe neba zimachitika zampila iZi
Pepa neba
Wofa lero safa mawa
Congrats
“Coach denies transfer rumours” Noma players are staying coz Bullets is the big team” watero coach wa noma kkkkkkk
ganyu yapindula
Thanks God mwatikondela
Dungah Patrick hihihihi
Wa Nyerere.. pamene sukumvetsa ndiye pati? Nyasa BiG Bullets 1 Nomad 0.. kugoletsa kukuvuteni, kuvomeledza kukuvutanso?
Neba uphunzirepotu apa. Ife taluza sitinapange chipolowe, tavomereza koma iwe ukaluza eeeeeeeee ngati akuchosa moyo. NOMA team ya ntendere.
Kodi Paja Mwaluza ?
Tangolawa kuluza.
awo anali mawu anakufedwa ampingo pitilizani mwambo wa maliro
ndlbe problem neba paja pa bingu sumaluza & vuto nd amene NAYO adabesha kkk maule oye the pple tme yova zawathu ake
Nde’yake!!! #the_Palestinians
Atigwera
Wamkaka maule
Ine kumwa milk
BB ndi Chi team ichi chondivetsa kukoma
BB NDI TIM YAFUK MUNGAKANE?
Fool time.
Noma yaona n’dulidwe wa kuchipatala kkkk
it is done, BB for lyk. Nkhumba Zonse Chigodola, Namikozo Fc usiye zodalira Mankhwala.
Yankhula neba nthawi yako ..nawe paja umalira zikakuvuta hahahahhaahah
MmMmm sazapezekanso mmm azingolunza mpaka 2090
Musachite matama maule,munakomoka inu masiku apitawa apa tangokupatsana chfk mumamvetsa chisoni
Wasogola mchikwama neba pa BB sungamake ife tangoyamba Silver,Moyale kwenikweni Mzuni ikupheratu Ha ha ha ha
Bullets more fireeeeee!!!!!!!!!
AhaaAaaa Bullets now where is adevel now he gone with
Tobias Njeula, tsopano walilatu kikikikikiki
From today Noma must learn to respect their Superios(Bullets)
Kuwinako lero mpaka timve kuwawa ndi mpira uwu umadana ndi mkwiyo zabwino zonse a bb
ifeyo anoma tiesetsa kulimbikira nthawi ndiyoculuka zazikulu zicitika
Ndili ndi mantha mzimu uja suwusa mu mtendele mayooooo ineeeeeee
paja mumawina pakakhala ma points, pakakhala ndalama imawina ndi noma.
Adzisiya!
Aaaaa kodi pa Log table muli part?
Koma relo wina wafa double ndithu kkkkkkkkkkk mahule eeeess
Kkkkkkkkk he he he he
Asasamba aluza
Better!! Amaonjeza kwambiri!!!! Big up my team!
Kumenyedwa ndi bullets mwati sichiyambi cha tsoka ? Lol
Wankaka
TAVOMELEZA KM MASO ALI PA MAKAZ
KOMA Ine ndikhale phee, koma nbb ndi deal
noma singachinye Bullets mu League.
maule 4lyf
Neba pepani kwambiri sitizapangaso
Congrats to my one and only BB
Zimachitika ine Nyerere ndi kuti Neba ulemuwako. Noma 4 lf
Amayakhula kwambiri akuti pa Bingu siinawineko ndi noma and yet is a new stadium hahahahaha
wamkaka maule
Aaaaa inu
Wina wamwa wamikozo ndangondutsamo sinatcholemo khwani kkkk umangoxiwilat.
Sindikuchiona chimene a bullets akusangalalira cos 28-21=7 whch means u nid more than 3 games
usovA
Usove ndiweyo neba
nkhani ndi game ya lero …mpila watha bwanji nde nkhani yaketu 1-0 kkkkkkk
hahaha ife tapeza 3 points inu neba? gat a reason to smile
Iwe sukuona kuti mukuchotsela pamenepo
Abambo, pamene simukumvetsa nde pati? Nyasa BiG Bullets 1 Nyerere 0 Kugoletsa kukuvuteni.. kuvomeleza kukuvuteninso?
Musovenge neba ife tilupita chisogolo kkkkk
Mbomba ife takukwatani vomelezan
Ma game atatu ukuwachulukitsa ndi iweyo
Kkkkk zavuta kupanda basi abro kkkkkkk
Mvuto la neba sum’mafuna kutiona tikukondwa… Mumalolera ana kumakumenyani koma mukafika pa ife kulumira mano… Iiiiii koma ongalukira kulimbikira.
Ife olo tisatenge bola silver itenge basi komaso 9years mu tnm pa BB Noma osawina komaso 13 years osatenga tnm kkkkkkkkk zampila
Ndiyekuti bb samenya magame atatu?
pama game 3 yoyamc tiyomwe tamenya naweyi more fireeee
Wina alira BB ndi nyatwa! !!! Kkkkkkk
Maule ndi maule. Inu mumati mpaka liti?
Wina wake ndinamuona atavala zovala zake za makaka a Orange amvekere Noma yanyamuka !!
Masewera Ena Tipatsire
Mpira tu ndi pa ground, osati zomwe mumalankhulazo.Mukuti bwanji tsopano all the best Big Bullets.
After such ACRASH I’pe “NYASA BIG BULLETS”has crealy demonstrated that amatha kulanga timatimu tamwano kkkkkkkh!!!….
Bullets aionesa noma n’dulidwe wa kuchipatala kkkkk
Maullleee woyeeee,nyerere zonse kuuna
Bullets pa 1 nonse a noma panyapanu mumalankhura kwambiri kuli kusadziwa maule kuti buuu
Man mpaka kutukwana!?
paja bullets imadziwika ndi umbuli
Takulelekani & just keep quite
Ndinanena ine kuti mamuna nzako ndichulu maule mofire
Is what I was expecting
Hahahahahaha foni ya #neba_ili_voicemail
This z motherfucken bulshit..Osman need 2 step down..asshole.
Lero kunalibe wokodzera pagolo kapena wogulitsa kanyenya wankhumba? hihihihihih
Dj nyimbo……shonongo…
Ndidzingorira ine wamaule wina asandifuse
Noma yamwa nkaka wankhumba kut swoooo!!! Zakuvuta neba.
Ndi kudya mazira ankaka lelo ativa madzi
NEBA WAPHWA LERO
Ma player ambirimbiri koma bibi yokha yokha basi winning is not having all players in the world even if you buy messi noma will never improve because of poor administrators
Ana amadelera
Pita ukoo iwe zangochitika mwa Mwai Noma for life
Eya ndi ana a cheapa kkkkkkkk
Thank You Jesus Christ!,am hape for my beloved team~bullets fc.
Chi team chaine …mauleeee.!!
Kodi noma ilibe ma striker abwino? ngati zili choncho mukanabwelekera Sindi Simutowe kapena Emma Zagada.
Ukunama iwe wamenyedwabe kkkkk pepan vuto si ine infuse zoya kkkkkk
Wamkulu simumenya zambiri
kkkkkk wina akulimbana ndi log table APA ngat anamva kut tikufuna patop…. patop pali inu koma take care ayeni ake apomwe mulipo akubwera…… uyooooo!!!!!!! makani Neba…….
wina akufuna logtable…kkkkk. tell him dat logtable izabwela after 30 gamez..that wil b best logtable.not now..kkkkkk .uzionaaaa
zoya
Neba konse konse wameza chule ? kkkkk
Tazisiya ma blues
mawule omwewo!!!
Well done.
bulets yandimvetsa kukoma neba yankhula zija unkayankhula padzana kkkkkk
It Woz 50 50 Game Its Just A Victory To BB
Mu TNM Super League Anawa Achepa
kma noma imandvesa kukoma bwanj muzpangapanga zmenezo zoluzazo
Ma poits alibe tchito inu anoma simungatene reaque kukhala patsolo sikupambana ai patsogolo mpambuyo pomwe
Mumat game mwasewela kale dzuro lero mumangakwanlitsa,mumakwanlitsa zimenez nemba tkakumana Ku Bar tkamwe shuter iwe uzikamwa mindol bs Nbb kt buuuuuu
Inetu Bullets ndisiya kuyisapotano chifukwa ndiye indimangisa kkkkkkk. Komano aneba wo akupuma???
Siya
Kkkkkkk mwati chani
AKANE AKANE ALOLE ALOLE…KOMA NEBA 0 – 1 the pplz tm
Mako ndi mako samasintha olo atatchoka mwendo kkkkk bb mpatali muchi zula amat mikhizeee
Akatundu omanga nd mawaya osamanya mwano mafana
pepa neba vomereza kuti mwaluza
LOGTABLE MUIONA KKKKKK MULI pa top a billets ndi 28 points ife a noma 21 koma ma game ndi 12 aliyense
Second round will be ours
Kkkk just work hard,it is possible bro
pemphera kuti Silver iluze,, iyo ili ndi 11 games koma 23 points… chimoto kuti bhuuu
Mighty. Mufulira wonderers 2 v city of lusaka 2..
sizinathe Goodluck,,,manoma amasokosa kwambiri amenewa kkkkkkkkk
The peoples team deserves a win. The boys played very well
Ma Palestine woye
we hw made it
congrats bb
Nebayi Sadzawinapa Pa Nbb, Ameneyi Ndimkazi Wathu.
wamkaka basi
History continues that Noma in league it’s our breakfast,lunch and dinner
Neba tamu umbudza, Neba tamuphiriphitha, Neba tamukwapula, Neba tamupala mamba, Neba tamusukuludza, Neba tamumeta mpala…..
hahaha ndili phee kumwelera milkit after bullets kundigwilira ntchito eeiishh
Ifetu kumangonva kukoma ndi mauleeeee mpano mpa theba capetown (Mitchellsplain woodland) kkkkkkkkkkk koma sulira koma ukafika kunyumba iwe
Kulongolora kwambiri Ana ayaya amaziona ngat afikapo, wakwiya ndi mfitiiiiii
Kikkkkkk ndi mfwitii osati mfiti…
ndye mpira bac Zatha
tiwonetseni log table tione ngati Bullets yafika pa top kungowinira phuzo basi noma for life
yes noma 4lyf
We have started shamelessly noma performance
kkkk kodi ngati ndi phuzo? koma ndikuwina kaya. logtable izatulu pakazatha 30 games. that will b best logtable
mmmmm vomerezan takuswan munkat chan
Bola takumetani mpala nd galasi opanda madzi kkkkkkkk
Ife olo tikhale chitseka log table bola takunyenyani….Dj nyimbo..shonongo….
Kumavomeleza neba, it doesn’t matter it’s one nil or five nil, win is a win. What matters is 3 points.
Noma for life … zangochitika mwa mwai kuti akanganya inu muwine
Ncy job 4 eva bb
Bola takuchepesera ulendo neba kkkkkkkkkk
Kkkkk osangovomela bwanji anyelere kkkk mukusika pang’ono ndi pang’ono basi
NEBA WACHITA MWAMWAYI KOMA UNALIMBA NAZO!
Moyo ngolimba nazo kumene Dj …mdara wachauya…
Big bullets …the peoples team.
Wakhaulabe
Uko kunali kuli kwa akuchikazi kkkkk poti alephela kuwinila phuzo,ngati ndi phuzo nkhondo tamenyela Silver basi.
Takuphulisani tnanena kale kuti tizapha tokha inu. Muzitimenya ma bonanza omwewo basi.Zamwayizo muchosere. Mene tamenyera muja munganene zoti ndimwayi? Mumamvera pa radio simunawonere. muli ndi mwayi kumenyedwa 1 yokha.
Tasung’unula mtolo kwa neba kkkkkkk
musayiwale paja kt ukazolower kuphwanya fupa nd ukadyako mnofu umasangalala kwambir,,, nde tiye nazo neba nthw ndiyako iyi
Kudya monona mwa neba kkkkkkkkk maule woyeeeeeeeeeeeeeeeeeeeee
Muli buaj bwana……
Kkkkkkkkk Mwateronso Bwana?
Kkkkk nangoti ndikupaseni moni basi…
Kkkkk Ok
Maule Moto Kt Buuuu!!! Evengelist Samuel Paul Butao Nyamzy Luka Waku Nsanje Chimwemwe Macheso Fanuel Kadulira Amos Makhuludzo Maneno Nyoni Blessings N Makhuludzo Mary Tchapu Jeicii Gomes Martha Mendulo Blessing Chikwapa Nesie Wa Ausman Brandy Mphatso Mchenga Jc Mbala Prosper Wyford Gideon Wa Kizito Frank Samy Tsamdoka Sterah Basho Nyamizinga Elizah Mafighty Malapane Leah Samu Gazi Md Hasan
Mwamuna mzako mpachulu mkulinga utakwelapo
Anna achepa!!!!!
big up maulle!!!!
Neba ndikuzapsa mtima pamene paja kkkk
Tamwaso mkaka bas
Mpila ndipa ground noma phokoso too much choncho mungatenge league
congrats NEBA!!!!!!!!!!!
Eeeeee koma NOMA mpaka pamenepo!!! Ee yandimvetsa kukoma bwanji.
#Zoya
Timwe wa MKAKA Tsopano!!!!
Kodi new catch yawo ija mumati Black mamba inalowa..?
Sorry NEBA umalongolora kwambiri
Amangotha yapakamwa basi pa ground 00
Kkkkkkk wasova
Kodi gyz game yatha bwanji tandiuza.
BB ndi ku chikweza babaa!
BB for life
Best team is knwn by its performance, we ar the best, ndkuzwa kt cmuyakha cfkwa mwapsa mtima,,,, neba upsa mtima osamalimbana nd mitchana Welford White Mateyu Yahya Kananji Edoh Malikebu Bosco WaLicia Misheck Gie Ftieh Phwadah Kenneth Kemah Mangazi Jnr Blessings Chibaya
Timafuna kuti neba nawe usuntheko ufike pa 21points usathe mawu
kk bola takuphan hahah
Ndiposo ameneyi osangonyadira kuti walaura bwanji
why do people overrate chester? he did nothing. nkwate is far much better than him. I want this shit to stop. mkwete is like Martial to me. young n talented. chester kumangothamanga ngti headless chicken? noma ili ndi mbwelera zama player. chande did nothing. I saw him trying to greet one of the BB players when he was substituted. his hand hit the air. he was even embarrassed. that guy is a traitor. noma fans u can cry n cry. ndikudziwa zikukuwawani. inu mazoba eti
Ife tu timavomereza mwasanga than winawe ha ha ha wangomukhumba chande kodi dzulo mwatenga league
Noma for life. Still on top kkkkkkk
Wina afune asafune tamwanso wa mkaka, zamuwawa akakolope nyanja
zili bho!.
Mkakankaka! !! BB
We are very far behind with football in Malawi RVG sananame ayi.
Tili pa mbuyo pa ma kwinako mumalizitsa
ana achepa auzeni azipita azikayamwa
Paja mwafikano pa top???
Ndiposo mwina afika di ali pa number 1
viva mauleee
Hahaha mawa ntchito ndigwila mutima pheee bb hoyeee kumudzi uko moni moni moni bb hoyeee
nyamuuuu B-) maule kulanga mafana!more fire!!!
MAULE WAMKAMKAAA
muli boo neba! mwawina.
Changa chisoni kwa neba waziona umat bwa! saiziya ntaun mwa iziwa bwa! maule woyeeeeeee ! zilibho nanga mulipat BB ndilande yavuta koma nde timba woyeeeee!!
BB Yomweyoo!
Neba!!!
zimachtika
Pepani za mpira sindimasitsata pepa nditu
MANOMA mukut bwanji? tatukwanani tioneso apa
Zandimvekera I Lovo kobasi BB BLESSEDBULLETS
noma sitikufowoka
Ndipo akangolowa Chande tikuphula basi game imeneyi.
Ndipo sindingafooke team noma basi
Akuti Noma itenga league machitidwe ake amenewa?
Ai koma machitidwe a bullets ndi omwe atenge ligi
Silver itenga zimenezi basi osati Bullets
Ai koma bullets
Wana Nacy itenge ndi Silver ija zimenezizo
how far are bb to noma ??? even thuogh u hv win but hhmmmmmm much behind
Ine wa silver moti apapa kugonja kwanuku zakhala bwino kwabasi kwa ife asilver
Tiyeni tizingopenya
Ndava pamenepo koma inuyo mmalankhula zochuluka kwabasi muvekele titenga league kuti mzimu wa …. Uwuse mu mtendere mwaiona lero game zikwanjetu
Mmmmm kungogwera
Kkkk koma iwe wabodza eti
Nancy umaleka kugwera Inuit bwanji
MA game a wiri omwe mwawina mu league mchifukwa chan mapernalty 1.Red Lions
2.Chitipa
Noma mway otenga league chilungamo chimafunika ukunka kachepa
Paja a Noma kulankhula amatha ngati 90 Min yakwana kkkkk
Amaiwala kuti pa malawi pano paliso azawo omwe amazitsata
Eg ma LIGI amawalephera
Ndaonaso choncho
Ubwino wake tili pa top be kodi league atenga dzulo abullets
Muli pa top koma mwayi otenga league ukunka kachepela chepelabe
iyi nde yanyekela basi
Bullets for life
Ohhhhhh,,,,, yaphunthwa
kkkkkkkkkk
woyeeee nanga pano ukutha bwa
ine kumva kukoma bb more
Last whisle
Tumwe tumwe kerry gold…..
Realy!!? Thats Great!
maule!!!!
Team ya ma star each & every season koma league osatengako, poor Noma viva bankerz
Big bullets woyeeeerrr
Madzi akunikika pamenepo
Umakwana Malawi 24
More fire
maule
Dailyboard loading………….
Noma iluza gemuyi
H stagestruck