President Peter Mutharika has axed Information Minister Malison Ndau and replaced him with vocal ex lawmaker Nicholas Dausi, Malawi24 can confirm.
This has been confirmed in the seen chief Secretary to the Government George Mkondiwa being replaced by Lloyd Muhara.
Mkondiwa has since been redeployed India as High commissioner. He replaces Dr. Issac Munlo who will now be Chief Director in the Ministry of Foreign Affairs and International Corporation.
Mutharika has made several changes to his cabinet atleast three times this year alone.
WE HAVE MORE REACTIONS TO COME.
Gud move
Asa mmwana tsopano kikikikikik
Mwanaaaa
Ma recycle onkhakha dziko silizathekaso kod nzeru ndiomwewa
kkkk dziko lino linadzaza ndi anthu amamina mmutu okhaokha sitingatukuke,,,,they keep on recycling old fashioned people to hold ministerial positions,,,period
Selious
Zadziko Mzosiirana Andau Mungopita Ku Mcp. Nao Adaus Adatopesa Nthai Ya D R Banda , Muluz, Bingu , J B Lero Kwa Pitala Ooooooooooo Ngat Kulibe Wena2
Athyape chingerezi mix with bodza kkkk, ndale eeish!…
prombonious Dausi extriocles the cabinet…. guys!!!!!!!
Kkkkkkkk
Kma kumenekoooo! madctionary m’manja mwni english wafka pampand tsopan,majournalist athu nkhaw iri biiiii
Thank u mr Ndau 4 the work, well done,,mumatha koma Dausi amathetsetsa,,
dictionary yemweyo! kufunika kugula oxford advanced dictionary.
Sopano timve latin english.kkkkkk
si uja ankatinamiza uja wakumana nazo achita bwino kumukhapa
Kkkkk sorry Mr ndau The president is not sick alibwinobwino lelo kukuthilan malovu
are there no lawyers or journalists qualified for this position in this country that we have to put up with this mediocrity?
mtolankhani nkhawa kuti bii!
FAKE LAWYERS MUTHARIKA AND LUNGU
abusa abodza
Welcome back our vocalist Dausi
Dausie Information minister
“May ur xmas be free from quagmire …. let it be adoriferous, full of rampant cockistocracy, aggravated by the vitality of perambolity with the plumage of decapitation so that the new year will be congruental in as far as the mototiplity is concerned” Dausi happy festival quote
Please dont me kikilikiki ndakomoka kuseka
pang’ono pamenepo Francis akubwera kenako ufa ndi kuseka
Mr Ndau,life goes on don’t worry. Mr president, for taking in Dausi, Ihave seen you doing agood job for the 1st time. Mr Dausi welcome.
The bizarre statement moves away from political partisan rhetoric,,,,,,,, hahaha we will be hearing such statements on various radio stations now
All are corrupt get rich or die trying.
Ma bombastic ena ndabodza asamatinamize
Now the reporters u have to wash ur brain Mr dausi z back
dictionaries for sale…anybody?
Ndemwati Titenge Dausi Chifukwa Chakuvomerezedwa Kwa Access Of Information Bill,dpp Ndikatakwe Mmm
kkkkkkkk DPP woyeeee!!!!!!!!
Kwavuta tsopano !!! Madictionary ayende malonda tsopano
Its time now to buy old version dictionary.
Welcome mr bombersticated words brain igwire ntchito tsopano
WELCOME DVT!! I rily misd dis guy so much accompanied by his bombastic words.His wel articulated words.Aaah!ndale zifike pokometsetsa tsopano.
DPP yabweram zili booooo.
wlcome MR DAUS its long time we here u r voice , koma atola nkhan mulimbetu ndi chingelez ch an nkuluyu muzinva koma ?apa ndiye oxford dictonary izi khala pafupi chonde
A Bwampinidi! Whxew!
That a good move,
ndebwino ndmwamba umu
kaya ndi Dausi or Ndau ine palibe chomwe chisithe m’moyo mwanga but ku ma family kwa awiriwo aona kusintha or muzamuike Aunt Tiwo pa mphando umenewo changabe palibe
Kkkkkk
Dausi amakwana
Welcom Dausi kkkkk tinachisowa chingerezi chako
tinakusowani bwana
zomwe tikufuna ndichitukuko osati kudziwa kapena kulankhula English ya deep ai
Nanunso Amalawi 24 Mwanamapo Kanu Kachizungu Kosatira Dausi Ati(president Peter Mutharika Has Axed Infomation Minister) Kkkkkkkkkkk. Apatu Zikuonetsa Kunama Kwanu Zoona Apresident Angatenge Nkhwangwa Ndikukhapa Nduna Yawo?Ayambana Chani?Kkkkkkkkk Dausi Tiyenawo Aphunzitse Amalawi 24.
Welcome back Mr Dausi
Z english zake zmenez nd bill ya access of imformation igwira? Adaus chonde tizivana
Program ya #Tiuzeni_Zoona pa #ZBS ikoma tsopano
eeeya wakumana nazo, APM amadana ndi mabodza, mesa unkanamiza dziko kuti alibwino pamene anafa ziwalo ali ku USA, wauponda
Bravo bwana Dausi, wishing you all the best.
Welcum dausi ma radio akome
Mr Dausi tingoti well come back
Pachoka mzako pali mmalo kkkkkkkie ANDAU APM GOOD HEARTH LERO FIRE.
Koma a dausi uku kukhoza kumaliza kwao chifukwa zinthu zafika povuta chilungamo sungalimbane nacho ndiye poti adausi amalimbana ndichilungamo ndiye ntchito yawo chabwino
So bad
DAUSI NDIOYENERA PA UDINDOWO KOMA A NDAWU SANATEZE (ATI) MWINA NKUONA AWACHOTSA ANACHEPERA NDI MCP KU PARLIAMENT
Steve Pindamkono ma dictionary aja agwirenso ntchito kkkkk
Eeesh akuluakulu ndidambo__ welcome mr Daus koma lankhulan kut tonse tzimva bho kkkkkkk
will this change the fallen economy??? Rubbish
Kodi azingosankha a Kumpoto okhakha? Ndau ndi Dausi onse akumpoto
Choka naweso ndau mmesa mngwaku ntcheu t/a kwataine?
Dausi ndiwaku mwanza
Aaaa owooo?
Odi ndikasake Oxford dictionary yanga, zingayambe kumandidutsa
Kodi bwanji mmokonda kusakha madala paudindo?
another old blood,old experienced thief….indeed an experienced lier! Malawi sadzathekadi basi
Good replacement Mr president
Ee aDAUSI tinawasowadi, mtolakhan komzeka ndi akabwila pa views triangle.
Mr Ndau is a victim of access to information bill (ATI). He will be rememberd as the minister who brought the ATI bill in parliament despite his party not willing to pass it. The other thing mr Ndau being a reverend was suitable for this job of information minister. This post requires someone who is naturally a lier not some reverends who believe lying is sin.
Atolankhani nonse mukudziwitsidwa kut ndatsegula shop yamadictionary kkk
why appointing Dausi ? An advanced dictionariy is expensive now a days
kkk cholinga tisamave info bas kk eee
Ma dictionary m’manja tsopano!!
Kkkk yaa timvee chizungu cha deep tsopano, extravagancy , political stocatle kkkkkkk welcum mngerezi
Mwanena Chilungamo MR, ndpo zmatitengela time kut tiziwe chomwe wakamba mpakana mtu kuwawa
Kkkkk Cambridge english
Hehehe
Kkkk ndi munthu wamkulu
This is ivacumasbanisaction of which misbacvagasi underiscula welcome Dausi
Kkkkkkkkk atongola nkhani.
Go to ECG ndau that’s not a problem , papa will do it for you with anointing water and oil everything is possible
Kkkk koma zomakamba ma bombastic English ayi
Acording to my apabango he is good dausi,kkk ma dictionary manja guyz,akwarkwangu wafika,we have more reactions to come,dalayu amapangitsa dpp kumvetsa sugar.Ndi adala pa ndale,ndamufira.Kkk no quarry here kkkkk dausi mwini oxford,not pakachere dictionary imene ndau ama user.Kkk zilikuno
Atolankhani muzingothawa noka tsopano kkkk
Welcom mr bombastic
Konga Mwam’na wasankhidwaso ndi Bwampini
Bwan Ndau analakwitsa kuyankha zomwe a Chakwera anayankhula. Zomwe zinayankhula a ndunawa zinali zopanda nzeru.
I am actually phlegmatic over this scandalous news..just yesterday they were jubilating during the awards now you’re hacking him off the office??…this is hellish and helibent,helical cracking,..not this hedgehog…!! kkkk
ehe nde mwat Dausi? dikirani muone ndale zikome. Ndikale lija zinakoma . kkkkkkk M’dala amakometsa ndale uyu… Am not saying am happy with the firing of Ndau but I missed this vocal politician so much!
Kkkkkkkkkkk!
Kkkkkkkkkkk!
Kkkkkkkkkkk!
kkkkkkk..sukunama aisy..agule advanced oxford dictionary…kkkkkkk
uyu ndi big
Kkkkk zoonadi odala.
English is there fo communication so if u say somethng that people cant get u then ua a fool
kkkk, mwina achepesa kufunsa
sindinapite patali ndixul koma secondary level tinathana naye.my english teacher,said to me:simple english is gud english.ngati ena sakumva zomwe ukuyankhula ndekuti ndiwe mbuli.Dausi saziwa chizungu koma grik.
Though i av neva went to college/university,Dausi samaziwa english,i observed tht on questions&answers with mr dausi,mayb we must say he’s fluent in english
Kkkkkkk ma jounalist athu azchta mantha kukamupnga intrview.Dausi pa uminster of information? zli khenge!
Andau amayenera kukhalabe paudindowu.Kuikapo Dausi ndi mistake
Welcome anyungwi
kkkkkk…
Kkkk Daus woyeee!!
Nobody has fired Ndau. He has just ceased as minister..
Nde zitinso izi
Ok
Tinveno malilime-kkkl. Oooohky welkom back atati.
Atolankhani avutikeso ndi mafuso apa!
Atolankhani avutikeso ndi mafuso apa!
madictionary mmanja
No wonder is fired from cabinet, not because of poor performance but has no root’s in DPP and he is a Reverend by professional and DPP believe in Lie’s not in love
Not only DPP believe in lies but all political parties and its players
Sure propaganda to protect the President, so Mr Ndau can’t do that
Really?
Ndau ndindani? ha ha ha ha ha!! Tamufuseni ndauyo kuti kudela kwanthu wapanga chani ndichulungamo chakecho chiloweleni boma mmmm 0 pa 10 ndipo eee amuchita bwino akungodya ndalama osapanga chitukuko amene akuti osadziwa kunamayo
i dnt support it!!!
What about minster of sports?he is failing to open new stadium
Reason? Pliz, let us knw
kkkkk zizungusopano kkjkk
I missed Dausi realy
MWAMVERA KWA ZBS?
things falling apart
Yatha Ntchito?kkkk Kumasazika Kumuzi!
timveno ziyakhulo apa