Machinga police on Sunday nabbed three men for possessing ivory worth millions of Kwacha.
Machinga police publicist Davie Sulumba said the suspects were found with ivory weighing 42 kilograms valued at 36 million Malawi Kwacha.
He said the suspects – James Mwera, 38, Mavuto Giniford, 18, and Dominic Siza Nyorongo aged 24 – were arrested for the offence of possesing ivory contrary to section 91 as read with section 110 of National Parks and Wildlife Act.
Sulumba told our reporter that they followed a tip by well-wishers that the suspects were keeping ivory and were offering them for sale.
“Police officers and game officers pretended to be buyers as they went to the house of James Mwera and found four pieces of ivory weighing 42 kilograms,” said Sulumba.
“They offered the pieces at a price of 55 thousand kwacha per Kilogram.”
James Mwera is from Amidu village, Mabvuto Giniford comes from Maluma village both in the area of traditional authority Liwonde of Machinga district while Dominic Nyirongo is from Dutie village, traditional authority Mzikubola of Mzimba district.
Mesa paja kulibe misika ya minyangayo nde osangoisiya aziseweletsa bwanji, komaso mitengo mukuipeza kuti pamene msika palibe?
Business yotentha2 imeneyi evn government can benefit,nde kumaganiza bwno apolice not kugwra ntchto kut akukonden
Business yotentha2 imeneyi evn government can benefit,nde kumaganiza bwno apolice not kugwra ntchto kut akukonden
have two of them anyone who knows where to sell, inbox
Good job!! mwina njovu nkupulumukako.
Gvtment yalero akulimbana ndi kuiteteza njovu kuti zisamaphedwe malo moteteza miyoyo yaazanthu achilubinowa. Tiyeni tionepo kanthu apa.
It’s not only Malawi ikuwocha nyanga zanjobvu.
Nkhuku za wanthu ndiye kuotcha kubwezeletsa njovuzo zaku+eash kuntonda
Nkhuku za wanthu ndiye kuotcha kubwezeletsa njovuzo zaku+eash kuntonda
I want to give a testimony on how I get cured from HIV/AIDS. As I was browsing through the internet on how to get cured, I saw a man testimony praising DR patrick I never believe it before until I tried it and it really work for me am very happy right now may God bless him. this is an opportunity for you to get cured contact him via [email protected] and also you can contact on whatsapp number +2349057780302 THESE ARE THE DISEASE THAT.DR PATRICK CAN CURED. HERPES. HIV/AIDS. CANCER. LOVE SPELL VIRUS, LOW SPERM COUNT, SIGHT DEFECT AND LOTS MORE…..
Ngati mwaotcha anthuwo atayeni palibe umboni
Tiyambapo maphuzo nazo izi iya
yeeeee zoona mukulephela kwamanga anaba ndalama aja pano akuchita kumatchena sut mu police anthu openga
iiiiih nkhani zopeka izi ndithu…nyanga za njovu izo ndi zomwe zinaotchedwa ku Kenya….
Nanga akupha albinos muti nawo bwanji
Ndi deal imeneyo muli mchere ochuluka, nde olo mwaotcha mwapindulapo chani?
Nde mwaluzatu mpaka kuotcha malawi sazathekanso kukhomelerana tokha tokha Fucken police
Bwana Johnn Yassin,aliyense atati adzipha njovuzo poti mza mulungu sipangakhale ngozi kaya
Ndinadziwa agalu awa kut aotcha pomwe ena mamvuto alinawo akanachepa zimandiwawa munthu olengedwa ndi mulungu Njomvu za mulungu osat zawonso ayi
Mukumatipatsa Mikute Ya Nkhan Eti? Ndakuonani Coz Nkhaniyi Ya Dzana
mangani a cashgate osati anthu osalakwa.
What you say about cashgate,leav them
ARREST AND IMPRISON THEM THAT’S WHAT THEY DESERVE
Iwe ukuyankhula ngati wopanda nzeru bwa nanga akupha alubinowa bwanji sakuwatengera kuprison . Zikomere awa ……………. Kodi njovu ndi moyo wamunthu chofunika ndi chani.
bora mukanasiyira eniwake agulise. muli ndi nsambi kungoranda m’kuotcha, anapeza movutikira + mwamanganso? wina apezera mavuto nyanga izi!! ndiye inu mufunetu m’sika muzikagulisa muzigura chimanga muzitipasa.tokha tikamazifunira mukutiranda tsono tizitani APETER ? apa ndiye mwaonesa ufiti wallah.
Kukaniza nyanga koma albino zazii
Kodi mwanva ndani,kuti njovu zake zasowa or zaphedwa,asiye nayo avaye nayo business yawo..
kodi mukuti 36mita,nanga mtengo umenewu ukuchokela kt popeza mukuti pa ziko lapansi palibe nsika wa nyanga,atayeni anthuwo bola kulimbana ndi awa akipha ma albinowa
nde tinene kut apapa mwaotcha 37milion kwacha?
kod bwanj mukumat worth of millions?mexa akuti padzko lin0 palibe nska wa nyanga.
Eeeeesh ma man anapita koma Babiloni? Iiiii ayi.