Kanengo Police in Lilongwe city are keeping in custody a 33 year -old woman for burning her husband’s private parts.
Deputy Public Relations Officer for Kanengo police Salome Chibwana identified the suspect as Juliet Chiwaya from Dedza district.
According to Chibwana, Chiwaya burnt her husband’s private parts after hearing that he was in a love affair with another woman.
The suspect boiled some water and poured them at the man’s private parts, burning her husband’s manhood in the process.
According to Chibwana, if the suspect is found guilty she will serve a maximum of seven years imprisonment with hard labour.
Police have since warned people to avoid solving conflict using violence. The security providers have also urged Malawians to report such matters to police before making stupid decisions.
Juliet Chiwaya hails from Malindama village in the area of Traditional (T/A) Authority Kaphuka in Dedza district.
Mpakana kuotchedwa ,anakumanapo akazi okha okha
Eeee too bad.
Pa nkhani iyi ndikupempha ma bungwe kuti achitepo kathu mpaka nkhani iyi ithe macilungamo mayiyo alangike ndithu.Kupanda kutero izi zipeleka nkhaza kwambiri kwa azibambo.Nzopweteka kutimwamuna wapwetekeka azimayi azipanga coment zonyasa.Mwamuna ndi mkazi azifanana mzose osati kumati Gendar pomwe mukukondera mkazi.

Waganiza bwanji? Bola kungochoka ena akanakutola koma apa mmmm wafa kawiri waluza mamuna kumangidwaso pompo olo mamunayo atakhululuka ukhala Naye bwanji zamanyazi
She must go to hell, coz sadziwa chomwe chipanga ubale,
She must go to hell, coz sadziwa chomwe chipanga ubale,
Ngati azibambo akuwonjeza nanunso musiye kuchinditsa. Stupid. Akakupangirani nkhanza mwamuna ndiye nkhani muma radio ndi manyuzi pepala monse. Apa poti wachitiridwa nkhanza ndi mwamuna ndiye mukusekerera. Koma chonsecho ngati mukulandira ulemu ndi chifukwa cha mwamunayo. Akanapanda mwamuna amene muli nayeyo bwanzi muli ndani inu? Osangothokoza kuti mamunayo anakuvuwulani mu nyansi za uhule munkapanga uja. Nayenso mwamunayo akachira adamuwotchenso kumaliseche mkaziyo tiwone ngati kudzakhale kokongola.
Makomenti enawa akutosonyezeratu kuti akuchokera mkamwa mwa mahule.
Palibe chachilendo apa akufuna kudya zakupsya chemwaliwo.
mesa ukufuna kuti akwatile mkazi mzake mayi opusa ameneyo fiti ya ikazi
Not good at all
Ndiye otchani amuna tosefe kuti inu akazi mukondwe
U did a gud job;i lyk u gal,it was too much for u being treated lyk a thrash
kkkk
Nah man
Guy ngati vikwati vavuta nikulekana mose mukali moyo than vamene mwayamba bantu baku malawi
Akuziwana asiyeni ngati mitu yanu ili pophwanyika kale ,I think that can not b repaired unafo ila kalee
mumaojeza amunanu nde mukapanda kusamala tidakakuotchan ma shaft
Nanuso azimayi muli ndibvuto that’s y amenyengera ena akazi iwe ungoti thambalaa ngati tabwa iyee
mmmmmmmmmmmmmm! kulakwatu kumeneko
Mai ameneyo 2points,amuna akuonjeza,atangommangira kusata lamulo koma zoona zake wacita bwino kuotcha cikumpangisa matamaco,kkkkkkkk
mukusangalala? amuna wose pa strike muzichindidwa ndi agalu poti ndizmene mmakonda azmay
as if mungakwanise mastrike anuwo
Must also be punished, why take authority on their hands.
Kunapsya bwanji inu anthu. Sanamete?????
Comment still loading……
pumbwa wachabechabe iyeyo ofunika kumthira tsabola ndithu
Mayi pamtumbo panu ndimaganizo opusawo
Just burn dat bitch olo nayexo angomuthira acid kwakeko!
Moto umapita kwatsala tchire. Kaya nde after apa ulowera kuti? Your guess is as good as mine.
Nawo amuna ena anasiya kalekale kuvala panti akazi amangootcha mnene afunira
Koma kukhala ine kutenthedwa AK 47 mkazi ndimlozatu serious
Ndikukhulupilira kuti ameneyu si mkazi olongosoka ndichihule chimenechi kapena kuti prostitutes ena timati mahosha
How can I explain this testimony to the public about a great man who help me out in serious illness I have HIV AID for good 3year and I was almost going to the end of my life due to the way my skin look like all I have in my mind is let me just give up because life is not interesting to me any longer but I just pray for God every day to accept my soul when ever I’m gone lucky to me my kids brother run to me that he found a doctor in the internet who can cure HIV online he help me out on everything, the doctor ask for my details, so he can prepare the herbal medicine for me from his temple after all he ask is done one week later I started getting more stronger my blood start flow normally for 4 to 5 days I start getting Wight before 6 days my body start developing my skin start coming up after 8 days which he told me that i will be completely healed, I went for HIV test and I was tested negative I’m so happy that I can say I’m not a HIV patient if you have HIV/AID or any sickness he can still help you in getting your ex-back to you please contact him via his email: [email protected], or whatsapp him on +2348143143878.
To hell u go,,, do u think we are too blinded to be fooled by ur stupid posts? Cheat ur fellow Nigerians not civilized Malawians! Never post ur nonsense on this page again! Mxiew
Mkazi waonjeza uyu mmmm ngati mwamunayo samamufuna osangochokako iyeyo bwanji kapena wapanga izi chifukwa cholira ndi kunyasa kwake kapena?
Well, for a woman to come to such a conclusion, sometimes amakhala watopa nazo. Amayi ndi munthu opilira.amakhala wayankhula kwa nthawi but no action taken. Nde amunanu mukamapanga zibwenzi ndi bwino kusaiwala kusamala pakhomo..mwina nkhani zoterezi zitha kuchepa..
not only kusamala pakhomo pamella koma kupereka ulemu kwa mkaz wao coz zkatere mkaz wawo amakhala chitsiru
Kwabas ndpo umakhalanso galu,,amuna ajaila kwabas!!
Atsikana Inu Kuotcha Shaft Ndikupha Kumeneko Nanga Adzatungaso Apa? Osamatero Ndi Engine Imeneyo Amasusira Iyeyo.
Mabungwe Zikanakhala Zandale Mudakava Kt Tivale Zofiila Tonse Tiyende Mmisewu Koma Apapa Dzili Cheteee! Panyapanu Amabungwe Tatapa Nanu Mmakonda Ndalama Kuotchedwa Staff Mpakana Mm
iiiii wapambana watani mamunayo mpaka ndikatenge nsambi ? odangochoka
nae mamuna anatani kunomuzika nayo kut asamuotche kkkkkk
mmalo motionetsa private parts you r bsy kutionetsa sign ya police….
mmalo motionetsa private parts you r bsy kutionetsa sign ya police….
Mmmm kulakwa kungosiyana mwamtendere bola koma osati kusiyana wina ataonongeka
Osaotcha Nyama Yantchire Kuisiya Osaidya,chomcho Mai Idyani Mwaotchadzo
Tsonotu wachita iyeyu eeee kuwotcha invetor kkkkkkkkkk wawonjezaa tsono iyeyono azikachaja kuti lumia yakeyooo.
Tsonotu wachita iyeyu eeee kuwotcha invetor kkkkkkkkkk wawonjezaa tsono iyeyono azikachaja kuti lumia yakeyooo.
Guinea 2___Malawi 1
Guinea 2___Malawi 1
Muwona nkhani imeneyo ithera m’malere popanda kuchuluka zoyangula pa media amabungwenso pamenepo ndei angoti ziiiii koma akadakhala wachitidwayo ndi nkazi pang’onong’ono wayangula amabungwenu ndalama zizakuphaaaa.kapena umafuna kunena kuti dzikoli ndi la akaziwaaaa????????????.

Waitha ameneyo enanu mutengepo phunzilo.
Waitha ameneyo enanu mutengepo phunzilo.
ameyo apolice tiyenayeyi ku court.
ameyo apolice tiyenayeyi ku court.
mpaka brai ?? amafuna adyele nsima or wat /??
mpaka brai ?? amafuna adyele nsima or wat /??
akuti sanagule ndiwo nde basi anangoti popeza soseji inali pafupi basi kuwocha kuti adyele kkkkkkkkkk
akuti sanagule ndiwo nde basi anangoti popeza soseji inali pafupi basi kuwocha kuti adyele kkkkkkkkkk
Ameneyo waitha azimunawa asamajaile iyaaaaaaaaaa!!!
Ameneyo waitha azimunawa asamajaile iyaaaaaaaaaa!!!
Ameneyo waitha azimunawa asamajaile iyaaaaaaaaaa!!!
Ameneyo waitha azimunawa asamajaile iyaaaaaaaaaa!!!
Banjanso lathera pomwepo
Banjanso lathera pomwepo
Uzaleka iwe ukupanga Comment yopusa Uhule eti
Uzaleka iwe ukupanga Comment yopusa Uhule eti
kkkkkkkkkkkk mamunayo anapusa motan kut mpaka amutenthe malo obisika ????
ngati sitikumvetsetsana m`banja ndibwino kungolekana mwachilungamo kma osati kuonongana miyoyo`enanu mukuti amuchita bwino alingati brother wanu mungamve bwa shame on you
ngati sitikumvetsetsana mmbanja ndibwino kungolekana mwachilungamo kma osati kuonongana miyoyo`enanu mukuti amuchita bwino alingati brother wanu mungamve bwa shame on you
ayayayayaaaaaaa!
Azibambo anyanya mbolo kuchita kunyamula m’manja ngati galu
Kkkkkkkkkkkkkk
bwanji kusowa kwa nyama???
bwanji kusowa kwa nyama???
[READ MY STORY. ON HOW I GOT MY HIV CURED].
Truthfully, i was tested HIV + positive for the past 8 years. I keep on managing the drugs i usually purchase from the health care agency to keep me healthy and strengthen, i tried all i can to make this disease leave me alone, but unfortunately, it keep on eating up my life, this is what i caused myself, for allowing my fiance make sex to me unsecured without protection, although i never knew he is HIV positive. So last Two Months i came in contact with a lively article on the internet on how this Powerful Herb Healer get her well and healed. So as a patient i knew this will took my life one day, and i need to live with other friends and relatives too. So i copied out the Dr Collins the traditional healer’s contact and I contacted him immediately, in a little while he mail me back that i was welcome to his Herbal Home whereby all what i seek for are granted. I was please at that time. And i continue with him, he took some few details from me and told me that he shall get back to me as soon as he is through with my work. I was very happy as heard that from him, as i was just coming from my friends house, Dr Collins called me to go for checkup in the hospital and see his marvelous work that it is now HIV negative, i was very glad to hear that from him, so quickly rush down to the nearest hospital to found out, only to hear from my hospital doctor called Browning Lewis that i am now HIV NEGATIVE. I jump up at him with the a test note, he ask me how does it happen and i reside to him all i went through with Dr Collins. I am now glad, so i am a gentle type of person that need to share this testimonies to everyone who seek for healing, because once you get calm and quiet, so the disease get to finish your life off. So i will advice you contact him today for your healing at the above details: Email ID: [email protected] or you can also add him up on whataspp +2349036950737. CONTACT HIM NOW TO SAVE YOUR LIFE AND DOCTOR ALSO CURE ALL KIND OF DISEASE AND SICKNESS: [email protected] AS HE IS SO POWERFUL AND HELPFUL TO ALL THAT HAVE THIS SICKNESS.

As I always say nothing good will come out from our country so called the warm heart of Africa everything there is amess
As I always say nothing good will come out from our country so called the warm heart of Africa everything there is amess
da woman is a witch
da woman is a witch
wachita bwino kumuocha ndipo olo unakangodula katundu yense
wachita bwino kumuocha ndipo olo unakangodula katundu yense
wachita bwino kumuocha ndipo olo unakangodula katundu yense
wachita bwino kumuocha ndipo olo unakangodula katundu yense
Zikanakhala bwino akanadula wakoyo
ase wanga kumpeza sindigavutikenso ndikuocha ndigagodula mutu wakewo bas
Ngati pali chokhumudwitsa pa moyo wangawu ndiye ndimkazi,kulibwino kumangotenga ma takeaway,cash n carry basi akazi abanja anatha zinatsala ndizigawenga za akazi,amabngwe kuli ziiiiiii,zitsilu za anthu.
Same as mi u n i same
Eish
Kakakakkakkakakakaka kulibe juuuuuuuuu apa ulendo wina ndi inu #kfce ndizako #foster kakkakakakaakkaka
wamuchita bwino sadzanyenganso ameneyo
Kkkkkkkk
Kkkkkkkk
Lafote linakwana
Kusagula ndiwo pakhomo kumakhalila kanyenya mujumbo wakewake ndizimenezo, azimotolako juliet kkkkkkkkkkk wasalawinawe umbombo shupt konko
I cn see tht malawi is goin to be on fire vry soon, why in our days peaple take fire as best weapon to deal with peaple who do wrong to the them? The one thn u hv to knw is that” muyeso umamuyezela mzako pangatalike bwanji jst knw tht someone wil use the same measure.
Kkkkkkkkk nde waotcha machine osokela zovala!! Nanga zovala zikang’ambika asokela chani!!! Koma ma boko-haram achuluka mumabanja amatsiku ano shhhhiiiiiitttttt!!!!!
Killer! Please add another 7 years
Killer! Please add another 7 years
Please add another 7 years
Please add another 7 years
Ukaotche Central Govt Office Ndiye Chithandizo Chidzichokera Kuti?? Wadzipha Wekha Mkaziwe #ufiti
Ukaotche Central Govt Office Ndiye Chithandizo Chidzichokera Kuti?? Wadzipha Wekha Mkaziwe #ufiti
Saza Pondaso Machine Ameneyo, Bt Pliz Amuna Muzisamalira Ndimoyo Umenewo Usamaliren.
Saza Pondaso Machine Ameneyo, Bt Pliz Amuna Muzisamalira Ndimoyo Umenewo Usamaliren.
iiiih ziotchanani mesa paja munavomereza kuti pamavuto mtendere mudzakhala limodzi,,,,kaziotchanani ….koma #yona’s wife anali woupedzatu #ThreeDays yona ali mmimba mwa #nsomba koma mkazi sanamuchite kalikonse,,,koma azimai amasiku anooo mmmm….ziotchanani !!!!!!!

men abuse
men abuse
Chaniiiii???????
Chaniiiii???????
The man had no private parts i think we wouid rather call them public parts because of the wy he was using them,Shame
The man had no private parts i think we wouid rather call them public parts because of the wy he was using them,Shame
Hahahahahahaaa! Malawi walusa shaaaaa!
Hahahahahahaaa! Malawi walusa shaaaaa!
Koma Juliet mpakana pamenepo?
Koma Juliet mpakana pamenepo?
kkkkkkkkkkkkk zofuna mkazi wakeyo samamukwanira n if he neva wanted her amaleka kupanga divorce nkumakapanga phada wakeyo bwanji
Ngati waontcha banja nde kuti banjalo latha
Ndikudabwa Ndimantha Mayi Wawotcha Malo Obisika Ovuta Kuwapeza Anatsata Njila Ya Nji? Ukawi Umenewo
shame on u woman
Akanangozithotholako nkumayenda Max
revenge abro,burn her parts too
nkhaza ku abambo zimakhala zikuluzikulu komanso zoopsa kwambiri…..
Wakhoza waotcha dimba lake chifukwa amadyerera ndiena
kkkkkkkk.iwe Francisco ndiwe wotani ndinkhanza kaya zimenezo.wamupha ameneyo ka.
Abambo mulipo?mundipezere kachizulu mdzakalawe!kakafupi kamid body koyera chinainswa
Kkkkkkkkk.ndikachiyani cc* wangayo sakukwanila? ndiwe wadyera eti uzikhutitsidwa.zomwe wakambazo zonse mesa ndimomwe alili wakoyo ndiye ufuna mzulu bwanji?
Azandiphunzitse vimafiiti !
Azandiphunzitse vimafiiti !
Kkkkkkkkkkkkkkkkkk koma iwe.
Shameful
Eye zoona osaika katunduyo mchisa chake,ndiye mapeto ake ndi fire!!fire!!
Mmmm mwaononganso machine osulira ana abambo aja haha zikubwelera pakale pompaja phala likunama!
Wawononga bazuka! Koma ameneyu
kkkkkkkk private parts!
Kkkkk naye mwamunayo, anangosiya pamtetete mthumbwanazo? Kkkkkk amafuna apange kanyenya? Koma zinganunkhiretu kkkkkkk
Mkazi wachita bwino,kuotcha shaftyo imagwira ntchito ndazimai ena.Go ahead sister,burn more.Azimai enanu ngati aziMuna akukuzuzani burn Shafts .
Mkazi wachita bwino,kuotcha shaftyo imagwira ntchito ndazimai ena.Go ahead sister,burn more.Azimai enanu ngati aziMuna akukuzuzani burn Shafts .
Mmmm that’s bad things guzy
Mmmm that’s bad things guzy
Kkkkkkk Nkhaza Kwa Azibambo So Sad Newz
Kkkkkkk Nkhaza Kwa Azibambo So Sad Newz
nde mukuti engeen yanokola
nde mukuti engeen yanokola
Koma limbani ngwira ndi mooo
kkkkkkk iwe Llyod nkhani zinazi zomvuta kumvesa lol
Oooo!!! Gents!!!! We staying with BOKOHALAM in our Houses. Shame on her
Oooo!!! Gents!!!! We staying with BOKOHALAM in our Houses. Shame on her
azimayi nkhwilu kusowa kwa ndiwo zanyama mpaka kuwotchela mbolo kuti mdyele sima? eeee nkhwan watopesad
azimayi nkhwilu kusowa kwa ndiwo zanyama mpaka kuwotchela mbolo kuti mdyele sima? eeee nkhwan watopesad
Kukambilana could be the best way not killing each other maka khani za banja izi mmmmm titengepo phunzilo amene sitinaotchedwe ife
Kukambilana could be the best way not killing each other maka khani za banja izi mmmmm titengepo phunzilo amene sitinaotchedwe ife
Masiku omaliza ano tiyeni tisamale kuli zambiri zochitika kwabasi azimai analimba mitima.ife azibambo tili patsogolo kungofunika kudalila moyo uyu sagula kaya
Masiku omaliza ano tiyeni tisamale kuli zambiri zochitika kwabasi azimai analimba mitima.ife azibambo tili patsogolo kungofunika kudalila moyo uyu sagula kaya
oyaasss this place called Dedza is bringing tarnishibg image to Malawu
oyaasss this place called Dedza is bringing tarnishibg image to Malawu
TREBAKELA AMENEYO
TREBAKELA AMENEYO
Eeeeeee mbola ku woononga engine
Eeeeeee mbola ku woononga engine
oyaasss this place called Dedza
oyaasss this place called Dedza
Wat kind of woman is ths 1, if a man did somthng wrong, u suppose 2 sit down en dicuss abt de matters,wat is zat 2 burns him? Wat did u get after ?stupid lady eeeeish ??????
Wat kind of woman is ths 1, if a man did somthng wrong, u suppose 2 sit down en dicuss abt de matters,wat is zat 2 burns him? Wat did u get after ?stupid lady eeeeish ??????
mayo ine!!!!
mayo ine!!!!
atsikana mukuti zakusangalasaninu . akadakhala bambo anu mudakamva bwanji?
atsikana mukuti zakusangalasaninu . akadakhala bambo anu mudakamva bwanji?
Mnadziwa zoti ndi mchewa bax munthu sangapange zimenezo
Mnadziwa zoti ndi mchewa bax munthu sangapange zimenezo
Kkkkk network error basi
Kkkkk network error basi
kkkkkk kusekatu ngat zabwino . koma akaz ena
kkkkkk kusekatu ngat zabwino . koma akaz ena
ndikulakwa nkhani ingakule bwanji imatha ndikukambilana thats why anamanga khoti.
ndikulakwa nkhani ingakule bwanji imatha ndikukambilana thats why anamanga khoti.
Mmmm so bad,kkkk kukwatira nkulimba mtima
Mmmm so bad,kkkk kukwatira nkulimba mtima
Waswa chikho chomwe chimamupatsa madzi asowa chomwera ameneyo
Waswa chikho chomwe chimamupatsa madzi asowa chomwera ameneyo
Eish azimayi ndi chani?ufiti basi
Eish azimayi ndi chani?ufiti basi
zinali bwanji mamunayo anagona,analezela,anafa? mpaka kuotchedwa osamva aaaa
zinali bwanji mamunayo anagona,analezela,anafa? mpaka kuotchedwa osamva aaaa
Ouch`
Mkazi ameneyo ingomgamulani mulandu wa trizon basi coz she’s bushit she can’t burn her husband like so mxiewwwwwwwww !!
Mkazi ameneyo ingomgamulani mulandu wa trizon basi coz she’s bushit she can’t burn her husband like so mxiewwwwwwwww !!
Mamunayo ndiopepela kwambiri mpaka kuwonelela Matchabwada akuthilidwa Moto ndiye azikalongosola bwanj zakudya pogonazi
Mamunayo ndiopepela kwambiri mpaka kuwonelela Matchabwada akuthilidwa Moto ndiye azikalongosola bwanj zakudya pogonazi
chikondi ndi chofunika tiyeni tikondane banja ndilabwino timaliyipitsa tokha chifukwa chosowekera chikondi.
chikondi ndi chofunika tiyeni tikondane banja ndilabwino timaliyipitsa tokha chifukwa chosowekera chikondi.
Akazi amaphaaaaa mukunama inu
Mwamunayo ndi ofoira mpaka kumamuotcha akungoyang’ana? amuna ena ndi mbuzi ndithu!
Mwamunayo ndi ofoira mpaka kumamuotcha akungoyang’ana? amuna ena ndi mbuzi ndithu!
Tsonotu banja ndilomwe waliwaulalo ndiye akuganiza kuti wapindu ? Zimenezo nde ndzibwana !
Tsonotu banja ndilomwe waliwaulalo ndiye akuganiza kuti wapindu ? Zimenezo nde ndzibwana !
ndipo ukanangochotseratu azimuna mwaonjedza inu
ndipo ukanangochotseratu azimuna mwaonjedza inu
No! @Thandi Banda.obwezera ndimwiniwake mulungu osati ifeyo.
No! @Thandi Banda.obwezera ndimwiniwake mulungu osati ifeyo.
Mpaka kuotcha mmm mkaziyu ayi waononga makna eeee wadula msonga
Mpaka kuotcha mmm mkaziyu ayi waononga makna eeee wadula msonga
Omg!!! Poor boy,nanu amunanu mukumonjeza nowadays,so we learn through mistake oh Men be warned!!!!
Eeeee! koma mkazi ameneyi nkhani yake inali yotani mpaka kuipsereretsa engine room.
Eeeee! koma mkazi ameneyi nkhani yake inali yotani mpaka kuipsereretsa engine room.
Factory burned. Eish! No more manufacturing kids.
Amuna Musamatenge Ngati Mulonda Wapankhomo Komaso Azimayi Kumeneko Sikulanga Koma Kuonjezela Mavuto Mayiakukagwila Yosalipdwa Vuto Kuana
Amuna Musamatenge Ngati Mulonda Wapankhomo Komaso Azimayi Kumeneko Sikulanga Koma Kuonjezela Mavuto Mayiakukagwila Yosalipdwa Vuto Kuana
Akazi amapha iweee!!!!
Ukunamaaa!
Chomcho kumatiotcha tizikudulanibe manja demmetti
Chomcho kumatiotcha tizikudulanibe manja demmetti
Nayeso m,baleyo anazisiya pati kut jezebel aziotche moteromo.sory my friend ur happiness has gone for gud.
Nayeso m,baleyo anazisiya pati kut jezebel aziotche moteromo.sory my friend ur happiness has gone for gud.
Until burn his …. mmm where waz he ? Men lets be as a sodier plz!!!
Until burn his …. mmm where waz he ? Men lets be as a sodier plz!!!
Mai Woipa Uyu Bwanji!!! Kuotcha Engine Ndi Chimodzimodzi Kuthamangitsa Kazembe Kkkkkkkkk!
Ndombolatu…. sizikanayenera kutero. so sad.p
Nde banja latha waonongaso katunduwake
Nde banja latha waonongaso katunduwake
ndichifukwa chake peter akuna tizikwatilana amuna tokhotokha,”nanga izi nzabwino?” kkkkk
ineso zandsangalasa amuna continue mama angazazolowere ena ndi phuziro lawo
Zaka 7 zachepa, tisanamizanepo apa, adakakhala mchimwene wa2 bwezi tikumva bwanji
Ife Tizamata Kazenjeko Ndi Supa Guru Tizaone Ngati Uzalimve Kukoma
Ife Tizamata Kazenjeko Ndi Supa Guru Tizaone Ngati Uzalimve Kukoma Thandie?
Koma nayeso wawonjeza, amayenera kukambirana.
Hahahahaha! this seem to be simple, but trust me on this one, these women will be the ones to rule us soon. you won’t hear activist fighting for men’s rights. you will find someone saying that she should not be given a stiff punishment coz she is a woman bt had it been it’s a man,,, munakamva achina zodiak akukoka nkhani imenei
Mmm kungomutaya basi osalimbana nazo zoterozo koma kuotchako mmm sizabwino
Guys kungoti azimuna ena amaonjeza
kkkkkk ndiye iyeyo Esnat Mukhaleya wakeyo Akayima Azipanga Nawobwanji?.
Thus not punishment woman you have.
Yet you have accumulate an offen guilty to yourself.
Even when you seek presence of God. That guilty of what you have done will always be in your mind.
Devil is your master using you woman.
See now what benefit have you gain.
This woman is idiot
Kukhala Mmalawi ndkulimba mtima
mkadziyo amaganiza chani akaonongeka ku engine amati zida zokhonzera zizichoka kuti poti zomwe zimamukhonza ndi izi wazipanga ngati kanyenyazi shame on her
Apa amadziwa kti its end of the road which was very winding.knowing kti akapedzano zina zida,sophiscated ones.
Hahahahahha koma man
Hahahahahha koma man
that’s very bad ppl
‘!%#82%@9#&+(™¥]¢~℅`×^¥=®}¥¶ zopanda pake
Amawonje ameneyo achitabwino kumakhutitsidwa
Mmmmmmmmm i know this bitch
So sad
Azibambo mukutionjezadi
Zosakhala bwino
hahaha its for better for worse. dont run away ffom marriage just use bookkoo haram
Shame nkhani zomvuta
Sizinakhale bwino paja amati banja mkupilila akapilile basi bambowo limenelo ndebanjalo
Chakudya waotcha nde mkazio azidya chani poti banja limalimba mchakudya?
munyanya azimunanu, mumatenga mkazi wapakhomo ngati wopusa, simuziwa kuti nafenso ndi boko harram. kip it up go a head mwina kuphwanyisana mutu kungathe
mwina alindivuto mkaziyo
mwina alindivuto mkaziyo
Big up to the lady
Big up to the lady
Zochisilu vuto ndi mkazio nkhani yose nnikuiziwa
Zochisilu vuto ndi mkazio nkhani yose nnikuiziwa
@ florida w@ happened?
@ florida w@ happened?
kusekelela kuwotchana machende kuti nonse mukhale opanda mwamuna? mukathela kubala mwina muli kubala kale
kusekelela kuwotchana machende kuti nonse mukhale opanda mwamuna? mukathela kubala mwina muli kubala kale
Hule iwe ulibe mamuna paja ndiwe palowa ina ukhalira yomweyo
zaccitika kuti kodi
chibwana timakana ase sitikwatila
chibwana timakana ase sitikwatila
wash ur tongue @ julius.satan akugwila u cat control urself umangozindikila zachitika
wash ur tongue @ julius.satan akugwila u cat control urself umangozindikila zachitika
Only Heartless Women Can Do Such Satanic Habit, Osamudula Chala Bwa? Shame
Kupanda mbolo ndi machendewo a Harriet bwenzi mutakwatiwa inu?ukukhalila zomwezo pabanjapo ndiye uzisekelela zopusazo muotchetu wakoyo tione ngati ungakhale osachindidwa
kungosiana bwa tinakumana okula kula@ jimmy
kungosiana bwa tinakumana okula kula@ jimmy
kaya wolakwa nd ndan idont care abambo padziko pano akuonjeza
aphiri mwati bwanji?mutakhala inuyo bwaa?kkkkk
nditha kuona nsana wa njila bax @ laston
dziwotchani choncho ena mabanja akusoweni coz nafe tidziwopa kuti tikukwatileni.
Anakhala Wa Chita Ndmamuna Anakaseva 14 Yrs
Omenyela ufulu wa Amayi mukuti bwanji
Nde kunali kuphulikatu
U was suppose 2 leave yr husband nt 2 burn her nor matter he was cheating u with another woman or abusive 2 u
so bad
Zimayi Ali Bwino, Ndiwolimba Mtima Ngoyenera Ku Training Ya Usirikali( Mawula Prison) Moyo Wake Wose!
ish!!!
Muli inu mungatani mutanva wa chikondi wanu ali ndi chibwezi?Ndichinthu chopweteka komanso chowawa fukwa ndinjira imodzi yosakilana matenda.
Nkadzi sanalakwitse as long as he is still alive,olo galimoto kuti ikhale pansi,nokola engine shaaa siyiyendanso
Nkadzi sanalakwitse as long as he is still alive,olo galimoto kuti ikhale pansi,nokola engine shaaa siyiyendanso
Kaliati say something. You always walawala six much
Zingayambe kuiwalik Malawi 1-2 Guinea
Ok
Good job enanu mutengerepo phuziro,,,amuna simuva lyaaaa
Azimayi mukudyetsanso heavy poti zilibe muyeso?tizidindapo chidindo pochoka chikafufutika ngoz kuwaula kupalanga nkuthira mchere basi
Mmmmm sad news
No bail
Nkhani iyi wakanakhala kuti wapanga ndi mwamuna ndikukuuzani kuti ikanavuta kwambiri,bwezi iri m’maradio station onse mdziko muno ndikunja komwe.
Chmfiti cha mzimai!!! Chlango chake nae nkungomukhomela cheasel ku *** asazaiwonenxo!
Anakapatsaso winatu mwina akuluwo
Pamenepa tizit pali banja or latha ?
Shame on her,mpaka kuwotcha capital Hill”city centre”amangidwedi basi
Mmmmmmmmmm Kusowa Chkond
Wachitabwano kuwocha munthuyo iyeyo anali kuti.
Dats Already Killing Dem His Lifo! Kutetha Engineeeeeeee…Hiiiiiiiiiiiiiiiii~! Zoona Fiti Zazikazi Ndizolimbadi Heartmtimaaaaaaaa!…Achaaaaaaaaaaaaamwatiphaaaaaaaaa!
Amuonongela headquaters……
kkkk mpaka headquaters
Dats Already Killing Dem His Lifo! Kutetha Engineeeeeeee…Hiiiiiiiiiiiiiiiii~! Zoona Fiti Zazikazi Ndizolimbadi Heartmtimaaaaaaaa!…Achaaaaaaaaaaaaamwatiphaaaaaaaaa!
Masiku omaliza mulungu ananena kale
Ku dedza kulibe akazi a banja nanutso,ambiri timitu tawo sitiyenda bwino.
mpaka kumuotcha ngati akupanga zibwenzi osangosiyana bwanji,
Kodi malawi akupita kut ? Mmmmm koma zina zikamachitika munthu utha kuona ngat ukulota ndithu
problems @ its climax in malawi.i think time is over 4 us now.
Mmmmm…Malawi wabvuta sopano azimai akulimba mtima ngati aku #south Africa
Malawi sali safe amwene lero ndi izi mamuna waotchedwa shaft ….not long ago wina kwachimseu ake mabatire anachita motafunidwa ndi brother wake ….kukhalako tizitero
Izi sinkhaza2 koma ndimwambo wa anthu aku#DEDZA,#BALAKA ndi#MCHINJI …..azimayi amaboma ndatchulawa ndioopsya ngakhale Satan amadabwa nazo zochita zao
sanalakwitse wachita bho iye ama cheater ali ndi mkazi kupanga zibwenzi osathetsa banja ndikumnayenda ndi enao bwanji big up mama nxt adzaganiza kawiri ngati adzapangeso
Thats queit amazing mzimai wandibebera uyu sanalakwitse ai men of today r taking women as trash isaaaa mmene munkamutenga nkumuika pa door ma side chicks anali kutiko?? Y didnt u marry them?? Mashalabwadawo ndi omwe amawatuma azibambowa nde wachita bwino THUMBS UP MAMA i lyk that
U must think as a human being that’s y mmalephera kupeza mabanja u’r thinking capacity is very very low & i dont think this u’r coments can come from some1 with 6 senses may be u were abnornomal sometimes ago & u r not yet recovered shame on u
I agree wit u Winford this is inhuman..Am a woman and i cudnt go this far that’s barbalique .if the man was cheating there are many ways of solving the issue or better still let him go his way osati mpaka pamenepoThis woman is capable of taking someone’s life
kkkkkkkkkk ulibe mzeru ndi iwe wekha osaganiza. sory paja uli ndi 15yrs ukadzakula udzaona ululu wake munthu akamaku cheater while u r duing ur best to plz dat person
langa ndi funso kodi mmene amuotchamu angatotenso?
Mmmmm osangomutaya bwanji?mpaka pamenepo inuso kumabvomelexa my malawi where are we going? Mulowelelepo ambuye!eeishiiiiii
eya kulipo bcz ma hormos azivepa yapsa ndi engine yokha basi
Kkkkkkkkkkkk koma mzimai ameneu hahahahahaa wamupulumutsatu mamunau kuchiopsezo chotenga kachilombo ngati analibe kale kkkkkkkkkkk
Kkkkkkkkkkkk koma mzimai ameneu hahahahahaa wamupulumutsatu mamunau kuchiopsezo chotenga kachilombo ngati analibe kale kkkkkkkkkkk
nonsenu mzelu mulibe kuthetsa kwa mavuto a m’banja sikulangana chonchi mkadziyu mzeru alibe ngati banja linamukwana ndi kwabwino anakangomanga adzipita kwao kunalembedwa kuti mwamuna deserves to have more than one wife akadzinu khalani omvera mwamuna wanu…
danny. kuti analemba choncho.
Shaaa mpaka kuyasa marriage headqterz kkkkk
mwakwatira chiphona mchimwene
Mayooooo!
mayi ameneyo ndiwolimba ntima mpaka kumuotcha mamuna ku main switch kkkii
Nayo Ladyo Amukazinge Ndi Mafuta Akukoma Kumaliseche Ong’ambika Kalewo Ave Sawawa, A Court Pin Code Yigwile Job Apa No Bias .
Mumangoti nkhaza kwa amayi…izi sono ndi ufiti kwa abambo
kungomusiya banja zinatani? sily woman!! kudzikaikira bwanji?
Common these days
Iiiish not gud…
Mai Ameneyi Ndi Chimaphang’ombe
Mina im tired ndikumva bad newz in M’malawi each n everyday maka nkhani zootchana izi week singathe osamva kut wina wapsyaaa so sad√√
ndiye paja mumangolimbikira kumati nkhanza kwamayi.ndiye lero munenakuti chani?
iih Kaya Zawo Zimenezo,
Aziwotchana.
They Wil Knw The Truth…………..
Time of the end. If she was being abused or the husband had affairs why not leave the bustard alone and just WALK AWAY FROM THE MARRIAGE PEACEFUL?
kkkkkkkk mamunayo anachta kutan kt mpaka mkaziyo aotche equipments yoseyo???
Samangidwa ameneyo kma akanakhala mwamuna wapanga zimenezo akanati khaza kwa amayi.
kill that lady
Amuchita bwino amuna anyanya uhule
Akanaotcha chimwene wako akanachitaso bwino?
wasiya uhule wakowo
Mbuzi ina yapanga like comment yopusayo
Akanakakhala wamkazi ndi amene wachitidwa zimenezi mukanati chani?
Emmie usadzayankhulenso mau amenewo ukudziwa kuti kumoyo kumeneku,ndiye madzi amoto umawadziwa bwinobwino iwe.samala ndi macomment ako opusawa
Amunawo akumakapanga uhule ndi mitengo ukamati anyanya??kodi mamuna amatchedwa hule??udaonapo amuna akuima mminseu atavula ukamati anyanya uhule??Undiyankhe nsangansanga mafuso angawo ndisanakwiye kwambiri kkkk
its not fair koma mpaka kuotcha…… akanadula koma #team_emmie
Manase thus the fact
Chifundo thus y mukadali kuotchedwa coz mumangoona uhule watsikana wanu mumaubisa
Chabwino wamuotcha nanga azanyenganso ndikupha kumeneko walakwisa ngati amaona kuti mamunayo akulakwisa banja linakangotha basi pamenepo sazakwatilanso komanso sazabelekans ndindani amene angamakhale ndi munthu oti olo nkutota komwe sakutota akamati awa sabeleka amakhalat akumachindana nyumbamo koma mwayi wa ana pamakhala palibe ndiye watch out ndi timakoment tanu topusato ngati ndinu anzelu
iwe emm mmene umavalira muja siuhule umeneo,choka!
Nayeso amuotche nkhanza zimenezo
malawi each and everytime tikumamva nkhan zotero….. anyway nzimai ndi olimba ntima mpaka kumuotcha zida + ma batry mwamuna shame….
Zamanyazi!azimayi tatani?tiyeni tipemphrr amuna athu ngati akuchita zoipa.Mulungu amayankha osati kuwaotcha.
et man mpaka kumuotcha mwamuna… zoopsatu izi…
Sikulimba mtima koma kuipa mtima. Simunthu ndi chirombo mfiti yotheratu. Otere ofunika amugamule kuti ngakhale atatuluka asakwatilane ndiwina koma yemweyu. Zomwe waotchazo adzazisowe yekha. Shupit woman!

kkkkkkkkkkkkk. #dian thats true walankhula ngati siiwe nkazi. kulankhula kwabwino. iyeyo azikadyana ndi zomwe waotchazo kkk
kkkkkkkkkkkkk. #dian thats true walankhula ngati siiwe nkazi. kulankhula kwabwino. iyeyo azikadyana ndi zomwe waotchazo kkk
Watero!? Kkkkk!
ya kkkkk nanga iye akumuotcha mwa
ya kkkkk nanga iye akumuotcha mwamuna nde mkumuthawa ndupeza mwamuna wina nde ootchedwayo asiila ndan akhale wake basi
kkkkkk komaa”’ waotcha yekha adye yekha lol mmmmm
elicy adzidyele yekha ameneyo kufunika kumukakamiza banja lipitilire pamenepo
nanga mwamuna wakeyo akakana kuti ine mfitiyu ayii asadye zangazi mupanga bwanji”’ #aubrey lol
kkkkkkkkkkkkkkkkk better that because mwamunayo achitavkukana yekha bt chomwe ndaona ine sangakwatile nkazi wina because zakudya zaotchedwa apa nde winayo azapanga ulesi kudya zootcha wina
kkkk zootcha zayenera kukhala zaboh”’ hahaha dikila ena akangoziyesa nkazi wakeyo akazatuluka saza makaso kkkk
kkkkkkkkkk elicy iweso usazaotche wakoyo tizakukakamizan kut dyan kanyenyao
kkkkkk ine nzakazinga lol”’ kuchita kuwaza tima spice lol
kkkkkk ine nzakazinga lol”’ kuchita kuwaza tima spice lol
lkkkkkk royco msuzi mix kklkkkk koma nde tingapse bho
lkkkkkk royco msuzi mix kklkkkk koma nde tingapse bho
waziziwaaa” nde ndani angasiye kukanganiraaa”
waziziwaaa” nde ndani angasiye kukanganiraaa”
hahahaha but nzovuta elicy ena zootcha samadya
hahahaha but nzovuta elicy ena zootcha samadya
mwinaso zabwinozo zaotchekamo mwasala madzi …..hehehehe koma guyz amna fasani
mwinaso zabwinozo zaotchekamo mwasala madzi …..hehehehe koma guyz amna fasani
loster kkkkkkkkkkkk zabwino zathamo??? mmmm,zili mthank2
loster kkkkkkkkkkkk zabwino zathamo??? mmmm,zili mthank2
So sad!!!!!!!! ndiye akachira azikati ndi akazi anga ndithu atulutseni
Wakhululuka kale akuti ndi mkazi wake
Amunafee ndiye eeeeee
That is too bad to burn someones private parts. Judgement is not like that
Akuziwa kuti iye akayipeza kwina yabwino banja kkkk
Mwina Dhilu Kapena Ndiwo Zankhwiru Anatenga Nthawi Asanadye,aPolise Mphuma Bwanji?